Pular para o conteúdo
Publicidade

EKSODO 12

26 Ndipo ana anu akakakufunsani kuti, Mwambo umenewu ukutanthauza chiyani?27 Inu mukawawuze kuti, Ndi nsembe ya Paska ya Yehova, popeza pamene ankakantha nyumba za Aigupto anasiya nyumba zathu.’ " Kenaka anthu anawerama napembedza.

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também