Pular para o conteúdo
Publicidade

EKSODO 16

2 Mʼchipululumo gulu lonse linadandaulira Mose ndi Aaroni 3 kuti, "Kukanakhala bwino Yehova akanatiphera mʼdziko la Igupto! Kumeneko timadya nyama ndi buledi mpaka kukhuta, koma inu mwabwera nafe ku chipululu kudzapha mpingo wonsewu ndi njala!"

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também