Publicidade

Êxodo 3

13 Mose anati kwa Mulungu, "Ngati ndipita kwa Aisraeli ndi kukawawuza kuti, Mulungu wa makolo anu wandituma kwa inu,ndipo iwo nʼkukandifunsa kuti Dzina lake ndi ndani?Tsono ine ndikawawuze chiyani?"

14 Mulungu anati kwa Mose, "NDINE AMENE NDILI. Izi ndi zimene ukanene kwa Aisraeli: NDINE wandituma kwa inu.’ "

Veja também

Publicidade
Bíblia Online Bíblia Online

Bíblia Online • Versão: 2026-06-29_22-07-56-