9 Yehova anati kwa Mose, "Ine ndikuwadziwa anthu amenewa. Iwowa ndi ankhutukumve. 10 Chifukwa chake undileke kuti mkwiyo wanga uyake pa iwo ndi kuwawononga. Ndipo Ine ndidzakusandutsa kuti ukhale mtundu waukulu."
Publicidade

+581 estão orando agora.
Junte-se à corrente de oração.