Publicidade

Gênesis 1

4 Mulungu anaona kuti kuwalako kunali bwino ndipo Iye analekanitsa kuwala ndi mdima. 5 Mulungu anatcha kuwalako "usana" ndipo mdima anawutcha "usiku." Ndipo panali madzulo ndiponso mmawa pa tsiku loyamba.

Veja também

Publicidade
Bíblia Online Bíblia Online

Bíblia Online • Versão: 2026-06-29_22-07-56-