Pular para o conteúdo
Publicidade

Gênesis 12

17 Koma Yehova anabweretsa matenda owopsa pa Farao pamodzi ndi banja lake lonse chifukwa cha Sarai mkazi wa Abramu. 18 Choncho Farao anayitanitsa Abramu namufunsa kuti, "Nʼchiyani wandichitirachi? Nʼchifukwa chiyani sunandiwuze kuti ameneyu ndi mkazi wako?

Veja também