Pular para o conteúdo
Publicidade

Gênesis 14

18 Ndipo Melikizedeki mfumu ya ku Salemu anabweretsa buledi ndi vinyo. Iyeyu anali wansembe wa Mulungu Wammwambamwamba,

20 Ndipo adalitsike Mulungu Wammwambamwamba

amene anapereka adani ako mʼdzanja lako."

Ndipo Abramu anamupatsa iye chakhumi cha zonse anali nazo.

Veja também