Pular para o conteúdo
Publicidade

GENESIS 18

13 Ndipo Yehova anati kwa Abrahamu, "Nʼchifukwa chiyani Sara anaseka nʼkumati, Moti ine nʼkudzakhaladi ndi mwana mmene ndakalambiramu?14 Kodi pali chimene chikhoza kumukanika Yehova? Pa nthawi yake, ngati yomwe ino chaka chamawa ndidzabweranso, ndipo Sara adzabala mwana wamwamuna."

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também