16 Ndipo Yehova Mulungu analamula munthu uja kuti, "Uzidya zipatso za mu mtengo wina uliwonse mʼmundamu; 17 koma usadye zipatso za mu mtengo wodziwitsa chabwino ndi choyipa, popeza ukadzadya za mu mtengowu udzafa ndithu."
Publicidade

+581 estão orando agora.
Junte-se à corrente de oração.