Publicidade

Gênesis 28

16 Yakobo atadzidzimuka, anati, "Zoonadi Yehova ali pa malo ano, ndipo ine sindinadziwe." 17 Tsono anachita mantha ndipo anati, "Malo ano ndi woopsa ndithu. Zoonadi pano ndi pa nyumba ya Mulungu ndi khomo la kumwamba."

Veja também

Publicidade
Bíblia Online Bíblia Online

Bíblia Online • Versão: 2026-06-29_22-07-56-