15 Ndipo ndidzayika chidani
pakati pa iwe ndi mkaziyo,
pakati pa mbewu yako ndi mbewu yake;
Iye adzaphwanya mutu wako
ndipo iwe udzaluma chidendene chake."
15 Ndipo ndidzayika chidani
pakati pa iwe ndi mkaziyo,
pakati pa mbewu yako ndi mbewu yake;
Iye adzaphwanya mutu wako
ndipo iwe udzaluma chidendene chake."