Pular para o conteúdo
Publicidade

GENESIS 3

17 Ndipo kwa Adamu Mulungu anati, "Chifukwa wamvera mkazi wako ndipo wadya zipatso za mu mtengo umene ndinakulamulira kuti, Usadye.

"Nthaka yatembereredwa chifukwa cha iwe,

movutikira udzadya zochokera mʼnthakamo

masiku onse a moyo wako.

18 Mʼnthakamo mudzamera minga ndi nthula

ndipo udzadya zomera zakuthengo.

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também