Pular para o conteúdo
Publicidade

GENESIS 4

Kaini ndi Abele

1 Adamu anagona malo amodzi ndi Hava mkazi wake ndipo mkaziyo anakhala woyembekezera nabala Kaini, ndipo anati, "Ndi thandizo la Yehova ndapeza mwana wamwamuna."

25 Adamu anagonanso malo amodzi ndi mkazi wake, ndipo anabereka mwana wamwamuna namutcha Seti, kutanthauza kuti, "Mulungu wandipatsa mwana wina mʼmalo mwa Abele, popeza Kaini anamupha."

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também