Pular para o conteúdo
Publicidade

GENESIS 45

Yosefe Adziwulula kwa Abale Ake

1 Tsono Yosefe sanathenso kuwugwira mtima kuti asalire pamaso pa antchito ake ndipo anafuwula kuti, "Aliyense achoke pamaso panga!" Motero panalibe wina aliyense pamene Yosefe anadziwulula kwa abale ake. 2 Ndipo analira mokweza mwakuti Aigupto anamva. Onse a ku nyumba kwa Farao anamvanso za zimenezi.

3 Yosefe anati kwa abale ake, "Ine ndine Yosefe! Kodi abambo anga akanali ndi moyo?" Koma abale ake sanathe kumuyankha chifukwa anali ndi mantha kwambiri pamaso pake.

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também