Pular para o conteúdo
Publicidade

YOHANE 1

Yesu Mwana Wankhosa wa Mulungu

29 Pa tsiku lotsatira Yohane anaona Yesu akubwera kwa iye ndipo anati, "Taonani, Mwana Wankhosa wa Mulungu, amene achotsa tchimo la dziko lapansi!

34 Ine ndaona ndipo ndikuchitira umboni kuti uyu ndi Mwana wa Mulungu."

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também