41 Choncho chimene Andreya anachita ndi kukapeza mʼbale wake Simoni ndipo anamuwuza kuti, "Ife tamupeza Mesiya," (kutanthauza kuti Khristu).