Pular para o conteúdo
Publicidade

YOHANE 1

41 Choncho chimene Andreya anachita ndi kukapeza mʼbale wake Simoni ndipo anamuwuza kuti, "Ife tamupeza Mesiya," (kutanthauza kuti Khristu).

42 Kenaka iye anabweretsa Simoni kwa Yesu, amene anamuyangʼana ndipo anati, "Iwe ndiwe Simoni, mwana wa Yohane. Udzatchedwa Kefa" (limene litanthauza kuti Petro).

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também