Pular para o conteúdo
Publicidade

YOHANE 11

33 Yesu ataona iye akulira, ndi Ayuda amene anabwera naye akuliranso, anakhudzidwa kwambiri ndi kuvutika mu mzimu. 34 Iye anafunsa kuti, "Kodi mwamuyika kuti?"

Iwo anayankha kuti, "Ambuye tiyeni mukaone."

35 Yesu analira.

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também