Pular para o conteúdo
Publicidade

João 11

43 Yesu atanena izi, Iye anayitana ndi mawu ofuwula kuti, "Lazaro, tuluka!" 44 Munthu womwalirayo anatuluka, womangidwa miyendo ndi manja ndi nsalu za ku manda, ndi nkhope yake yokulungidwa nsalu.

Yesu anawawuza kuti, "Mʼmasuleni, ndipo muloleni apite."

Veja também