Yesu Aneneratu za Kuperekedwa Kwake
18 "Ine sindikunena za inu nonse. Ine ndikudziwa amene ndinawasankha. Koma izi zikukwaniritsa malemba: ‘Iye amene akudya nawo chakudya changa, ndiye amene anandiwukira.’

+581 estão orando agora.
Junte-se à corrente de oração.