Pular para o conteúdo
Publicidade

João 14

Yesu Njira ya kwa Atate

5 Tomasi anati kwa Iye, "Ambuye ife sitikudziwa kumene Inu mukupita, nanga tingadziwe bwanji njirayo?"

6 Yesu anayankha kuti, "Ine ndine njira, choonadi ndi moyo. Palibe munthu angafike kwa Atate popanda kudzera mwa Ine.

Veja também