3 Vinyo atatha, amayi a Yesu anati kwa Iye, "Wawathera vinyo."
4 Yesu anayankha kuti, "Amayi, chifukwa chiyani mukundiwuza Ine? Nthawi yanga sinakwane."
5 Amayi ake anati kwa antchito, "Inu muchite chilichonse chimene akuwuzeni."