27 Kenaka anati kwa Tomasi, "Ika chala chako apa; ona manja anga. Tambasula dzanja lako ndi kukhudza mʼnthiti mwanga. Leka kukayika, khulupirira."
28 Tomasi anati kwa Iye, "Ambuye wanga ndi Mulungu wanga!"