Pular para o conteúdo
Publicidade

YOHANE 21

Yesu Abwezeretsa Petro

15 Iwo atamaliza kudya chakudya chammawa, Yesu anati kwa Simoni Petro, "Simoni, mwana wa Yohane, kodi umandikonda Ine kuposa mmene amandikondera awa?"

Iye anati, "Inde Ambuye, Inu mukudziwa kuti Ine ndimakukondani."

Yesu anati, "Samala ana ankhosa anga."

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também