Pular para o conteúdo
Publicidade

João 21

Yesu Abwezeretsa Petro

15 Iwo atamaliza kudya chakudya chammawa, Yesu anati kwa Simoni Petro, "Simoni, mwana wa Yohane, kodi umandikonda Ine kuposa mmene amandikondera awa?"

Iye anati, "Inde Ambuye, Inu mukudziwa kuti Ine ndimakukondani."

Yesu anati, "Samala ana ankhosa anga."

19 Yesu ananena izi kumuzindikiritsa mtundu wa imfa imene Petro adzalemekezera nayo Mulungu. Kenaka Iye anati kwa Petro, "Nditsate Ine!"

Veja também