Ophunzira Abweranso kwa Yesu
27 Pa nthawi yomweyo ophunzira ake anabwerera ndipo anadabwa kupeza Iye akuyankhula ndi mayi. Koma palibe amene anamufunsa kuti, "Kodi mukufuna chiyani?" kapena, "Nʼchifukwa chiyani mukuyankhula naye?"

+581 estão orando agora.
Junte-se à corrente de oração.