19 Yesu anawapatsa yankho ili: "Zoonadi, Ine ndikukuwuzani kuti Mwana sangathe kuchita kanthu pa Iye yekha. Iye amachita zokhazo zimene amaona Atate ake akuchita, chifukwa chilichonse chimene Atate amachita Mwana amachitanso.
Publicidade

+581 estão orando agora.
Junte-se à corrente de oração.