Pular para o conteúdo
Publicidade

OWERUZA 14

3 Koma abambo ndi amayi ake anayankha kuti, "Kodi palibe mkazi pakati pa abale akowa kapena pakati pa anthu a mtundu wako, kuti iwe upite kukapeza mkazi kwa Afilisti anthu osachita mdulidwe?"

Koma Samsoni anawuza abambo ake kuti, "Kanditengereni ameneyu basi, pakuti ndamukonda."

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também