Pular para o conteúdo
Publicidade

Lucas 1

Aneneratu za Kubadwa kwa Yesu

26 Mwezi wachisanu ndi chimodzi, Mulungu anatuma mngelo Gabrieli ku Nazareti, mudzi wa ku Galileya, 27 kwa namwali wopalidwa ubwenzi ndi Yosefe, wa fuko la Davide. Dzina la namwaliyo linali Mariya.

Veja também