Pular para o conteúdo
Publicidade

LUKA 1

28 Mngeloyo anafika kwa iye nati, "Moni, inu amene Ambuye wakukomerani mtima kwambiri! Ambuye ali ndi inu."

29 Mariya anavutika kwambiri ndi mawu awa ndipo anadabwa ndi kulonjera kotere. 30 Koma mngeloyo anati kwa iye, "Usachite mantha Mariya, pakuti wapeza chisomo pamaso Mulungu. 31 Udzakhala woyembekezera ndipo udzabala mwana wamwamuna ndipo udzamupatse dzina loti Yesu.

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também