Pular para o conteúdo
Publicidade

LUKA 11

2 Yesu anawawuza kuti, "Pamene mukupemphera muzinena kuti:

" Atate,

dzina lanu lilemekezedwe,

ufumu wanu ubwere.

3 Mutipatse chakudya chathu chalero,

4 mutikhululukire machimo athu,

monga ifenso timakhululukira aliyense amene watilakwira.

Ndipo musalole kuti tigwe mʼmayesero.’ "

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também