Pular para o conteúdo
Publicidade

Luka 15:17,18

TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

17 "Maganizo ake atabweramo, iye anati, ‘Ndi antchito angati a abambo anga amene ali ndi chakudya chimene amadya nʼkutsalako ndipo ine ndili pano kufa ndi njala! 18 Ine ndinyamuka ndi kubwerera kwa abambo anga ndipo ndikati kwa iwo: abambo, ine ndachimwira kumwamba ndi kwa inu.

Em outras traduções

  1. NTNYBL2025 Nyanja

    17 Nambho njelu yapo zidayamba kumbwelela, wadajhikambila mwene, ‘Mnyumba mwa atate wanga muli mbowa zochuluka, izo zikudya chakudya mbaka kutaya, ndande yanji ine nife ni njala!’ 18 Nibwelela kwa atate wanga ni kwaakambila, ‘Atate, nakuchimwilani imwe ni Amnungu kumwamba.

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.