17 Nambho njelu yapo zidayamba kumbwelela, wadajhikambila mwene, ‘Mnyumba mwa atate wanga muli mbowa zochuluka, izo zikudya chakudya mbaka kutaya, ndande yanji ine nife ni njala!’ 18 Nibwelela kwa atate wanga ni kwaakambila, ‘Atate, nakuchimwilani imwe ni Amnungu kumwamba.
Publicidade