1 Asati lazima nikulembeleni, kwa nghani ya kwatangatila wandhu Amnungu yawo ali kumujhi wa ku Yelusalemu. 2 Nijhiwa umo muli ni mtima othangatila, nidajhielekela chindhu chimenecho kwa wandhu amujhi wa ku Makedonia. Nidakukambilani, "Wandhu amujhi wa ku Akaya ali ojhikonjekela kuyambila chaka chatha." Chimwecho mtima wanu ochocha wakoka wandhu ambili. 3 Chipano, naatuma achabale wathu yaani Tito niwajha wina awili kwanu, dala kujhidamila kwathu kwanu kuoneke kuti osati mau yachajhe, ni kuti mlitayali kupunda ni mthandizo wanu ngati umo nakambila. 4 Wandhu amujhi wa ku Makedonia yapo saajhe pamojhi ni iine sitidakuphezani simuli tayali, sitidalenga njhoni ife ni anyiimwe ndande siikhale takukhulupililani mopitilila. 5 Chimwecho naona kuti lazima napembhe wandhu anyiwa achogolele, aike bwino mbhaso yanu yaikulu iyo mudakamba simuchoche, nayo ilangiza zene kuti mbhaso iyo mwachocha mwaichocha kwa kukonda asati kwa kukakamizidwa.
6 Zindikilani mau yaya, uyo wavyala pang'ono wakolola pang'ono, uyo wavyala zambili wakolola zambili. 7 Kila mmojhi, chipano wachoche ngati umo wakhozela, kwa mtima asati kuchocha kwa kudandaula kapina kukakamizidwa, pakuti Mnungu wamkonda yujha wachocha kwa mtima kokondwela. 8 Mnungu wakhoza kukupachani anyiimwe kupitilila yayo muyafuna, dala mkhale ni kila chindhu icho muchifuna siku zonjhe, dala mpunde kuthangatila kwa kila njhito iyo ili yabwino. 9 Ngati umo yalembedwa mmalembo ya Mnungu,
"Iye wachocha kwa ubwino,
wapacha osauka,
ubwino wake ulama muyaya."
10 Mnungu uyo wampacha mlimi mbeu ndande yovyala niuyo wampacha chakudya, siwakupacheni mbeu izo muzifuna, siwazichite zimele, zikule ni kukupachani vokolola vambili va ubwino wanu. 11 Iye siwakuchiteni kupata kwa kila kandhu, dala kwa ubwino wanu wandhu amuyamike Mnungu, kupitila ife. 12 Njhito iyi yabwino iyo muichita siithangatila vofunika va wandhu a Mnungupe, nambho siichite wandhu ambili amuyamike Mnungu. 13 Wandhu sampache ulemelelo Mnungu ndande ya njhito iyi mwaichimikiza mwachinawene, ndande ya kukhulupilika kwanu kwa Uthenga Wabwino umfotokoza Kilisito, ndande ya ubwino uwo mwachitila wandhu a Mnungu ni wandhu wonjhe. 14 Chimwecho sakupembheleni kwa mtima onjhe ndande ya ubwino wa okha uwo wakupachani Mnungu. 15 Timuyamike Mnungu kwa mbhaso yake iyo siifotokozeka.