Publicidade

2 Coríntios 6

1 Tikakhala ochita njhito pamojhi ni Mnungu, tikupembhani kupunda msadavomela ujha ubwino uwo mwalandila kuchoka kwa Mnungu utaike chajhe. 2 Mnungu wakamba chimwechi,

"Ndhawi yokwana nakuvechela,

ndhawi ya uomboli nakuthangatila."

Chimwecho, ino nde ndhawi yofunika kulandila uomboli wa Mnungu!

3 Sitifuna kumuchekeleza mundhu waliyonjhe, dala utumiki wathu usadakhala wodandaulicha. 4 Mmalo mwake, kwakila kandhu tijhilangize kuti ife atumiki a Mnungu, kwa kila kandhu, kwa kulimba mtima kupunda kwa mavuto, machaucho ni kulaga, 5 tidabulidwa ni kumangidwa mndende ni kwa kukuwidwa pa ndhandala pakuchita njhito zolimba zolemecha, tachezelela ni kukhala popande kudya. 6 Tijhilangiza kukhala atumiki a Mnungu kwa mtima woyela, kwa malango, kwa kulimba mtima ni kwa ubwino, kwa Mzimu wa Mnungu ni kwa chikondi chopande ugunghuli, 7 kwa mau la uzene ni kwa mbhavu ya Mnungu. Kuvomelezeka ni Mnungu nde chida chathu cha kukengelela ni kuhundukila. 8 Ife timtumikila Mnungu wandhu akati lemekeza kapina kutudelela, tilaumidwa ni kutielekela. Tionekana amthila kumbe tikamba zene, 9 ngati osajhiwika kumbe tijhiwika kupunda, tioneka ngati omwalila kumbe ife amoyo. 10 Ingakhale talangidwa, sitidaphedwe, ingakhale tionekana tali ni chisoni, tikondwa, ingakhale tili osauka nambho tachita ambili kukhala opata, tioneka wandhu opande kandhu, kumbe tili ni kila kandhu.

11 Achabale Akolinso takamba namwe padanga, kwa kuku kondani kupunda. 12 Ngati kuli ni chindhu chalichonjhe chichekeleza kukukondani anyiimwe, ife sitidasiye kukukondani anyiimwe nambho anyiimwe nde mwasiya kutikonda ife. 13 Chipano nikamba namwe ngati wana wanga. Mkondane ngati umo ife takukondani anyiimwe.

Poolo wakaniza wandhu kulunjana ni wandhu samkhulupilila Mnungu

14 Msada gwilizana ni wandhu osakhulupilile Mnungu. Bwanji ubwino ni kuipa vikoza kukhala pamojhi? Dangalila ni mdima vikhoza bwanji kukhala pamojhi? 15 Bwanji Kilisito wakhoza kugwilizana ni Satana? Okhulupilila Mnungu wagwilizana bwanji ni osakhulupilila Mnungu? 16 Nyumba ya Mnungu igwilizana bwanji ni viboliboli va unami? Ife ni nyumba ya Mnungu wa moyo. Ngati Mnungu mwene umo wadakambila,

"Sinikhale pamojhi ni anyiiwo,

ni kukhala pakati pao,

Sinikhale Mnungu wao,

nao sakhale wandhu wanga."

17 Chimwecho, Ambuye Ambhavu akambanjho,

"Chokani pakati pao,

mkajhipatule nao,

msadaghafya chindhu choipa,

Nane sinikulandileni.

18 Ine sinikhale Tate wanu,

namwe simukhale wanawanga wachimuna ni wachikazi,

ine Ambuye Mnungu uyo nili nimbhavu nakamba."

Veja também

Publicidade
2 Coríntios
Ver todos os capítulos de 2 Coríntios
Bíblia Online Bíblia Online

Bíblia Online • Versão: 2026-06-18_14-04-22-