Publicidade

Lucas 12

Yesu wanyindila wandhu yawo ajhichita kuti amtumikila Mnungu

1 Ndhawi imeneyo, wandhu wochuluka yapo adasonghana mbaka amapondana, Yesu wadayamba kukamba ni oyaluzidwa wake, niwakamba, "Mkhale maso, musadachita ngati Afalisayo, yawo ajhichita kuti amchata Mnungu. 2 Palibe icho chabisidwa sichiikidwa padanga, ni palibe icho chavinikilidwa sichivukulidwe. 3 Chimwecho, icho mwachikamba kumdima, sichivekele padanga, ni icho mwachinong'ona mmakhutu kuvyumba vanu, sichiuzilidwe pandhandala."

Uyo wafunika kuopedwa

4 "Nikukambilani anyiimwe achabwenji langa, msadawaopa anyiyawo akupha thupi, anyiyawo pambuyo pa yameneyo saakhoza kuchita chilichonjhe. 5 Nambho, sinikulangizeni uyo mufunika kumuopa, muopeni yujha pambuyo pakupha thupi wakhoza kukuponyani kumoto wosathima muyaya. Zenedi nikukambilani, muopeni iye. 6 Bwanji, njhwala zisano sizigulichidwa kwa mtengo waung'ono kupunda? Nambho, pamaso pa Mnungu siiwalika ata njhwala imojhi. 7 Zenedi, ata machichi ya mmitu yanu, yawelengedwa. Chipano, msadaopa, anyiimwe nde muli ni phindu kupunda kupitilila njhwala!"

Kumuuzila ni kumkana Yesu

8 "Nikukambilani uzene, kila uyo wauzila pamaso pa wandhu kuti wali pamojhi ni ine, Mwana wa Mundhu naye siwamuuzile kuti mundhu mmeneyo wali pamojhi niiye pamaso pa atumiki akumwamba a Mnungu. 9 Nambho, mundhu waliyonjhe uyo siwanikane pamaso pa wandhu, Mwana wa Mundhu naye siwamkane pamaso pa atumiki akumwamba a Mnungu."

10 Waliyonjhe uyo wakamkambila mawu yoipa Mwana wa Mundhu, siwalekeleledwe, nambho waliyonjhe uyo siwamtukwane Mzimu Woyela, siwalekeleledwa.

11 "Yapo sakupelekeni mnyumba ya mapembhelo ya Ayahudi, kapina pamaso pa wakuluakulu ni alamuli kuti mulamulidwe, msadajhifunjha umo simujhitetezele. 12 Ndande yake, Mzimu Woyela siwakuyaluzeni icho simufunike kukamba ndhawi imeneyo."

Chifani cha mundhu wopata sabobwa

13 Mundhu mmojhi pakati pagulu la wandhu lijha, wadamkambila Yesu, "Oyaluza, mkambileni mkulu wanga kuti tigawane chuma icho adatilekela atate wathu." 14 Nambho, Yesu wadayamuyangha, "Bwenji wanga, yani uyo wanisanghula ine kuimilila ni kugawana kwanu chuma cha atate wanu?"

15 Ndiipo Yesu wadaakambila wandhu wajha, "Mujhipenyelele ni chipili vindhu vonjhe, pakuti umoyo wa mundhu siupatikana ndande ya kuchuluka kwa chuma icho walinacho mundhu." 16 Ndiipo Yesu wadapacha chifani, "Kudali ni wopata mmojhi uyo wadali ni munda uwo udabala vipacho vochuluka. 17 Mundhu wopata mmeneyo wadayamba kuganizila mumtima mwake, ‘Nichite chiyani? Pakuti nilibe malo yosungila chakudya changa icho nachikolola. 18 Sinigomole nghokwe zanga ni kumanganjho zazikulu kupitilila ni mmenemo, nde umo siniikemo vokolola vanga vonjhe ni chuma changa.’ 19 Pamenepo siniukambile mzimu wanga, ‘Chipano uli ni chuma cha mbili, ivo udavisunga kwa vyaka vambili. Pumulila, udye, umwe ni kukondwela.’ 20 Nambho Mnungu wadamkambila, ‘Wopusa iwe! Umoyo wako siutengedwe usiku uno. Ni vindhu vonjhe ivo wajhiunjikila sivikhale vayani?’"

21 Yesu wadakamba, "Umu nde umo ili kwa yawo ajhiunjikila chuma cha mbili mwene wake, nambho alibe chindhu icho chili chokhadwa pamaso pa Mnungu."

Kumkhulupilila Mnungu

22 Ndiipo Yesu wadakambila oyaluzidwa wake, "Chimwecho, msadajhichaucha kuusu umoyo wanu kuti simdye chiyani, kapina ndande ya matupi yanu kuti simvale chiyani. 23 Chifuko, umoyo ni wofunika kupunda kupitilila chakdya, ni thupi nilofunika kupunda kupitilila vovala. 24 Penyani khungubwe, izo sizivyala kapina kukolola, zilibe nghokwe kapina malo yaliyonjhe yosungamo chakudya, nambho Mnungu wazidyecha. Anyiimwe ni abwino kupunda kupitilila mbalami! 25 Yani pakati panu wakhoza kuonjezela umoyo wake ingakhale kwa saa limojhipe? 26 Pakuti, mlepela kuchita chindhu chaching'ono ngati ichi, ndande yanji mujhivuticha kuchita ivo vili vavikulu vimenevo? 27 Penyani maduwa umo yakulila. Siyachita njhito kapina kujhikhwadilicha, nambho nikukambilani ata Mfumu Solomoni uyo wadavala vivalo vabwino kupunda, siwadajhikadwiliche ngati limojhi la maduwa yaya. 28 Chipano, ngati Mnungu wayaveka nchimwecho maduwa ya kuthengo, yayo yamela lelo ni mawa yakugwa ni kutaidwa pamoto, bwanji, sisakuvekeni anyiimwe bwino kupunda, wandhu achikulupililo chochepa!

29 "Basi, msadajhisaucha mmitima yanu, kuti mukudya chiyani kapina mukumwa chiyani. 30 Pakuti yameneyo yachauchilidwa kupunda ni wandhu wonjhe yawo samjiwa Mnungu. Nambho, Atate wanu a kumwamba ayajhiwa kuti muyafuna. 31 Nambho, ufunefuneni uti ufumu wa Mnungu, ni vindhu ivi navo simupachidwe."

Kujhiikila chuma kumwamba

32 "Msadaopa, anyiimwe muli gulu laling'ono, pakuti Atate wanu akonda kukupachani anyiimwe Ufumu wao. 33 Gulichani vyuma vanu ni mwaninghe ndalama wandhu wosauka ndalama zimenezo. Mujhikonjele matumba ya ndalama yosatha ni ikilani chuma kumwamba icho sichichepa, kumalo uko anghungu sakhoza kuba ni vidudu kuwananga. 34 Ndande yake, yapo waikila chuma chako ndeyapo umoyo wako siukhalepo."

Khalani maso

35 "Mkhale tayali kupota njhito ni musiye nyali zanu ni ziwala, 36 Mkhale ngati atumiki yawo amlindilila bwana wawo uyo wabwela kuchokela ku ukwati, kuti yapo siwachakulize chicheko, amchakulile chisanga. 37 Mbowa wajha siakondwele mbuye wawo yapo siwapheze atomlindilila. Zenedi nikukambilani, bwana mmeneyo siwavale vivalo va mbowa ni kwakambila kuti mkhale niine sinikutumikileni. 38 Mbowa wajha siakondwele mbuye wawo wakaapheza ali tayali kumlandila ata ngati siwajhe usiku kupunda kapina mmalengakucha. 39 Nambho nifuna mujhiwe chindhu ichi, ngati mwene khomo wadakajhiwa ndhawi uyo wakuba siwajhe, wadakakhala maso, siwadakasiya nyumba yake igomoledwe. 40 Chimwecho, namwenjho mukhale wokonjeka nyengo zonjhe, pakuti Mwana wa Mundhu siwajhe ndhawi iyo anyiimwe simuiijhiwa."

Mbowa wokhulupilika

41 Ndiipo Petilo wadamfunjha Yesu, "Ambuye, chifani ichi chitihusu ife tekha, kapina kwa wandhu wonjhe?" 42 Ambuye adayangha, "Mbowa yuti uyo wali wokhulupilika ni wa njelu, uyo waikidwa ni bwana wake kwaimilila kila kandhu kake, kuti wagawile chakudya pa ndhawi iyo ifunika? 43 Siwakhale wokondwa mbowa uyo bwana wake yapo sabwele sampheze niwachita chimwecho. 44 Nikukambilani uzene, siwamuike waimilile vindhu vake vonjhe. 45 Nambho, ngati mbowa mmeneyo siwaganizile mumtima mwake kuti mbuye wake wachedwa kubwela, ni kuyamba kwamenya mbowa wina yawo waimilila, wachimuna ni wachikazi, ni uku niwadya, ni kumwa ni kulojhela, 46 bwana wake siwabwele siku ilo siwalijhiwa iye. Siwampache chilango chachikulu kupunda mbowa mmeneyo ni kumuika pamojhi ni wosakhulupilika."

47 "Mbowa uyo wajhiwa ivo afuna bwana wake, nambho siwachita yayo afuna bwana wake kuti wayachite, mbowa mmeneyo siwalangidwe chilango chachikulu kupunda. 48 Ni mundhu waliyonjhe uyo siwajhiwa icho chifunika kuchita, niwakachita vindhu ivo wafunika kulangidwa, siwapachidwe chilango chachiang'ono. Pakuti, mundhu uyo wapachidwa vambili, siwadaidwe vambili, ni mundhu uyo wapachidwa ulamulilo waukulu ni mundhu mwina, siwafunjhidwe kopitilila."

Yesu wapeleka kupatukana

49 "Nafika kujha kukweleza moto pajhiko, ni ine nikhumbila kuti udakakhala wathokwelela! 50 Nambho nili ni mavuto yayakulu yayo nifunika kuti nivutike, nambho nichauchika kupunda mbaka yapo siyakwanile! 51 Msadaganiza kuti najha kupeleka mtendele pajhiko la panjhi? Notho! Najha kupeleka kupatukana. 52 Ni kuyambila chipano, wandhu asano ambadwa umojhi siapatukane, wandhu atatu siabulane ni wandhu awili, ni awili sabulane ni wandhu atatu. 53 Atate siapatukane ni mwana wao, ni wana wao sapatukane ni atate wao, amayi sapatukane ni mwana wao wamkazi ni mwana wao wamkazi sapatukane ni amayi wake, ni mpongozi wamkazi sapatukane ni apongozi wake wakazi."

Kujhiwa nyengo

54 Yesu wadalikambilanjho gulu lijha lawandhu, "Yapo muona mitambo niyachokela kumpoto, kwamkamojhi mkamba kuti vula siinye, ni ikunyadi. 55 Ni yapo muona mbhepo kuchokela kunyanja, mkamba kuti sikukhale kofunda, ni ikhaladi chimwecho. 56 Anyiimwe agunghuli! Muzijhiwa nyengo kwa kupenya mlengalenga, chifuko chiyani simjhiwa mate ya vindhu vichokela saino?"

Uvane ni adani wako

57 "Ndande yanji mlepela kulamula mwachinawene icho chili chabwino? 58 Yapo upita ni mdani wako kunyumba ya milandu, ujhitaidi kuvana naye muli mnjila. Ngati siuchita chimwecho siwakupeleke kwa mbhavu kwa mlamuli, ni mlamuli siwakupeleke kwa asikali ni asikali siakuike mndende. 59 Zenedi nikukambila, siuchoka mndende mbaka yapo siulipile ndalama yothela."

Veja também

Publicidade
Bíblia Online Bíblia Online

Bíblia Online • Versão: 2026-06-19_11-20-24-