1 Wadalipo mchogholeli mmojhi wa Chiyahudi, wa ghulu la Afalisayo, jhina lake Nikodemo. 2 Siku limojhi usiku Nikodemo wadamchata Yesu, wadamkambila, "Oyaluza, tijhiwa kuti imwe oyaluza yao mwatumidwa ni Amnungu, pakuti palibe mundhu uyo wakhoza kuchita vizindikilo ngati ivo muchita popande Amnungu kukhala pamojhi naye."
3 Yesu wadamuyangha, "Uzene nikukambila, mundhu ngati siwabadwa kakawili siwakhoza kuuona Ufumu wa Amnungu."
4 Ndiipo Nikodemo wadamfunjha, "Mzee wakhoza bwanji kubadwanjho? Siwakhoze bwanji kulowa mmimba mwa amaye wake nikubaadwanjho?"
5 Yesu wadayangha, "Uzene nikukambila, mundhu ngati siwabadwa kwa majhi ni Mzimu, siwakhoza kulowa mu Ufumu wa Amnungu 6 Mundhu wabadwa chithupi kwa atate wake ni amake, nambho wabadwa Chizimu kwa Mzimu woyela. 7 Siudadabwa pakuti nakukambila kuti lazima kubadwanjho. 8 Mbhepo iputa ni kupita uko ifuna, uvela mvekelo wake, nambho siujhiwa uko ichoka kapina uko ipita. Nde umo ili kwa mundhu uyo wabadwa kwa Mzimu woyela."
9 Nikodemo wadafunjha, "Siikhozeke bwanji vindhu ivi?"
10 Yesu wadayangha, "Bwanji, iwe ni oyaluza olemekezedwa Izilaeli, ata chimwecho siuvijhiwa vindhu ivi? 11 Uzene nikukambila, ife tikamba yayo tiyajhiwa, ni tifotokozelela vindhu ivo taviona, nambho mau yathu simuyavomela. 12 Ngati nakukambilani vindhu va pajhiko la panjhi, namwe simudakhulupilile, simukhulupilile bwanji nikakukambilani vindhu va kumwamba? 13 Palibe mundhu uyo wadapitapo kumwamba, nambho Mwana wa Mundhu uyo wadachika kuchokela ku mwamba."
14 Ngati Musa umo wadaipachikila njoka pamtengo kujha ku phululu, nde umo Mwana wa Mundhu nayo wafunika kupachikidwa, 15 kuti kila uyo wamkhulupilila wakhale ni umoyo wa muyaya. 16 Mateyake Amnungu adaakonda wandhu a jhiko la panjhi ni kumchocha Mwana wao wa yokha, kuti kila uyo wamkhulupilila siwadatayika, nambho wakhale ni umoyo muyaya. 17 Mate yake Amnungu siwadamtume Mwana wake kuti walamule wandhu a pajhiko la panjhi, nambho waombole kupitila mwana wao.
18 "Uyo wamkhulupilila iye siwa lamulidwa, uyo siwamkhulupilila watho lamulidwa, ndande yosamkhulupilila Mwana wa yokha wa Amnungu. 19 Lamulo lene nde ili, dangalila wajha pajhiko la panjhi, nambho wandhu akonda mdima kusiyana dangalila, ndande vochitika vao ni voipa. 20 Waliyonjhe uyo wachita voipa waliipila dangalila, siwakhoza kujha kudangalila, pakuti siwafuna vindhu vake vijhiwike. 21 Nambho yawo achita uzene akujha kudangalila, kuti vichito vao vionekele padanga kuti yachitika kwa kwaavela Amnungu."
22 Pambuyo pa yameneyo, Yesu wadapita ku Yudea pamojhi ni oyaluzidwa wake. Wadalongeza nao kumeneko, niwabatiza wandhu. 23 Yohana nayo wamato kwa batiza wandhu kumeneko ku Ainoni, pafupi ni ku Salimu, pakuti kumeneko ndeuko kudali ni majhi yambili. Wandhu amapita kumeneko ni kubatizidwa. 24 Ndhawi iyi Yohana wadali wakali osamangidwe mndende.
25 Padachokela mtafu pakati pa oyaluzidwa akumojhi a Yohana ni Myahudi mmojhi kuusu chikhalidwe cha kusamba pa kuvomelezeka kumlambila Mnungu. 26 Ndiipo, oyaluzidwa achameneo adamchata Yohana, ni kumkambila, "Oyaluza, mundhu yujha wadali pamojhi namwe muchija la mchinje Yolodani yujha mdamchochela umboni, nayo wabatiza ni wandhu onjhe atomchota!"
27 Ndiipo, Yohana wadaayangha, "Mundhu siwakhoza kulandila chilichonjhe popande kupachidwa kuchokela kumwamba kwa Amnungu. 28 Mwachinawene mkhoza kunichochela umboni kuti nidakamba, ‘Ine osati Kilisito uyo wasanghidwa ni Mnungu, nambho natumidwa kuti ni mchogholele!’ 29 Wammuna wa ukwati nde uyo wamkwata mwali wa ukwati. Nambho bwenji wa uyo wakwata uyo waima pafupi naye ni kumvechela, wakondwa kupunda yapo wavela mvekelo wake. Iyi nde Ndande ya kukwanila kwa chimwemwe nchanga 30 Kilisto uyo wasanghidwa ni Amnungu ifunika walemekezedwe kupunda, ine nichike."
31 Uyo wasanghidwa ni Amnungu kuchokela kumwamba ni wamkulu kupitilila vonjhe, uyo wachokela pajhiko la panjhi ni wapajhiko la panjhi, niwakamba vindhu va pajhiko la panjhi. Nambho uyo wachokela kumwamba ni wamkulu kupitilila vonjhe. 32 Iye wakamba yajha wayaona ni kuyavela, nambho palibe mundhu uyo wavomela umboni wake. 33 Nambho mundhu walionjhe uyo wavomela uthenga wake, wachimikiza kuti Amnungu ni azene. 34 Uyo watumidwa ni Amnungu wakamba mawu ya Amnungu, mate yake Amnungu ampacha mundhu mmeneyo Mzimu wao popande chipimo. 35 Atate amkonda Mwana ni amningha vindhu vonjhe. 36 Uyo wamkhulupilila Mwana wa Amnungu wali ni umoyo wa muyaya, uyo siwamvela Mwana siwakhala ni umoyo wa muyaya, nambho siwakhale mumkwiyo wa Amnungu.