1 Jhumaapili umawamawa, kukali kosache, Maliya uyo wadachokela ku Magidala wadapita kuchiliza, wadapheza mwala wachochedwa pakhomo la chiliza. 2 Ndiipo wadathamanga msanga mbaka kwa Petulo ni oyaluzidwa mwina uyo wadakondedwa ni Yesu, wadamkambila, "Alichocha thupi la Ambuye pachiliza, sitijhiwa uko aliika."
3 Petulo pamojhi ni yujha oyaluzidwa mwina adapita kuchiliza. 4 Onjhe awili adathamanga, nambho yujha mwina wadathamanga msanga kulekana ni Petulo, wadachoghola kufika kuchiliza. 5 Yapo wadakwatama ni kuzuzumila mkati, wadaona sandape zaikidwa, nambho siwadalowe mkati. 6 Simoni Petulo wadajha, wadalowa mchiliza, mmenemo wadaona sandape zaikidwa, 7 ni chitambaa icho wadamangidwa Yesu kumutu. Sichidaikidwe pamojhi ni sanda, nambho chavilingidwa ni kuikidwa pachokha. 8 Ndiipo oyaluzidwa mwina uyo wadachoghola pa chiliza, wadalowa mkati wadaona ni kukhulupilila. 9 Adali akali osajhiwe Malembo Yoyela yayo yadakamba kuti idali lazima wahyuke. 10 Chimwecho oyaluzidwa adabwela kukhomo.
11 Nambho Malia wadaima pabwalo pa chiliza, wamatolila. Yapo wamalila, wadakwatama ni kuzuzumila mchiliza, 12 wadaona atumiki akumwamba Amnungu awili avala njhalu zoyela mbee, akhala yapo lighonekedwa thupi la Yesu, mmojhi kumutu mwina kumyendo. 13 Atumiki akumwamba achameneo adamfunjha malia, "Maye, ndande yanji mulila?"
Wadamkambila, "Waachocha Ambuye wanga, sinijhiwa ukoaikidwa!"
14 Yapo wadakamba yameneyo, wadang'anamuka kumbuyo, wadamuona Yesu waima pamenepo, nambho siwadajhiwe kuti nde Yesu. 15 Yesu wadamfunjha, "Maye, ndande yanji mulila? Mumfunafuna yaani?"
Malia wamaganiza osunga busitani, wadamkambila, "Olemekezedwa ngati imwe nde mwaatenga, pepani nipembha munilangize ukomwamuika, sinimtenge."
16 Yesu wadamkambila, "Malia!"
Malia nayo wadang'anamuka, wadamkambila kwa Chihebulania, "Laboni" Mate yake "Oyaluza."
17 Yesu wadamkambila, "Usadanigwila, ndande nikali osapite kumwamba kwa Atate. Nambho mapita kwachabale wanga ukaakambile. Nipita kumwamba kwa Atate wanga ni Atate wanu, Amnungu wanga ni Amnungu wanu."
18 Chimwecho Malia uyo wadachokela ku Magidala wadapita kwaapacha nghani oyaluzidwa naona Ambuye, ni kuti wadamkambila chimwecho.
19 Idali ujhulo siku lo yamba la jhuma. Oyaluzidwa wake adakomana pamojhi mkati mwanyumba, vicheko vidachekedwa ndande ya kwaopa achogoleli wa Ayahudi. Ndiipo Yesu wadajha kuima pakati pao, wadakambila, "Mtendele ukhale kwanu!" 20 Yapo wadakamba yameneyo, wadalangiza manja yake ni ndhiti yake. Chimwechi oyaluzidwa wake adali ni chimwemwe kupunda kwaona Ambuye. 21 Yesu wakambilanjho, "Mtendele ukhale kwanu! Ngati Atate adanituma ine, nane nikutumani anyiimwe." 22 Yapo wadakamba yameneyo, wadaapumbuzila mpuyo ni kwakambila, "Landilani Mzimu Oyela. 23 Mkaalekelela wandhu machimo yao, wandhu achameneo sialekeleledwe, mkasia kwalekelela volakwa vao nawo salekeleledwa."
24 Nambho Tomaso, uyo wamatanidwa Mawila mmojhi wa oyaluzidwa anyiwajha khumi ni awili, siwadali pamojhi nao yapo wadajha Yesu. 25 Ndiipo, oyaluzidwa wina adamkambila, "Taona Ambuye." Nambho iye wadaakambila, "Nikasiya kuona mawala ya mizumali mmanja mwake ni kubiza chala changa mmawala ya mizumaliyo ni kubiza jhanja langa mundhiti mwake, sinikhulupilila."
26 Chimwecho, pambuyo pa masiku nane oyaluzidwa adalinjho pamojhi mujha munyumba, ni Tomaso wadali pamojhi nao. Vicheko vidamangidwa ni kuima pakati pao wadakamba, "Mtendele ukhale kwanu!" 27 Ndiipo wadamkambila Tomaso, "Jhanacho chala chako upenye manja yanga, jhanalo jhanja lako ubize mundhiti mwanga. Msadakhaikila, nambho khulupilila!"
28 Tomaso wadayangha, "Ambuye wanga ni Amnungu wanga!"
29 Yesu wadammbila, "Bwanji unikhulupilila ndande waniona? Apachidwa mwawi anyiiwo sadanione, nambho akhulupilila."
30 Yesu wadachita vizindikilo vina vambili pachogholo pa oyaluzidwa wake ivo sividalembedwe mu chikalakala ichi. 31 Nambho ivi valembedwa dala mkhulupilile kuti Yesu nde Kilisito, Mwana wa Amnungu ni kumkhulupilila mkhale ni umoyo wa muyaya kwa kukhala mkati mwake.