1 Pambuyo pa yameneyo kudalipo ni phwando la Ayahudi, nayo Yesu wadapita Ku Yelusalemu. 2 Kumeneko ku Yelusalemu, pafupi ni chicheko icho chitanidwa chicheko cha mbelele, kudaliko ni thiwi ilo kwa mkambo wa Chihebulaniya, Betizata, ilo lidazungulilidwa ni khumbi zisano. 3 Mkati mwake mudali odwala ambili, osapenya, andendele, ni ovuwala. Amalindilila majhi yavundulidwe, 4 pakuti ndhawi za mbili mtumiki wa kumwamba wa Amnungu wamachika ndhawi zina ni kuyavundula majhi. Mundhu waliyonjhe uyo wachogolela kubila mmajhi yayo yamavundulidwa, wamalama ndhenda yaliyonjhe iyo wamadwala. 5 Ndiipo, pamwepo wadalipo mundhu mmojhi uyo wadali odwala kwa ndhawi ya vyaka selasini ni nane. 6 Yesu yapo wadamuona mundhu mmeneyo wagona pamenepo ni kujhiwa kuti wadakhala kwa ndhawi ya itali, wadamfunjha, "Bwanji, ufuna kulama?"
7 Nayo wadayangha, "Wakulu, ine nilibe mundhu onibiza mthiwi majhi yapo yavundulidwa. Yapo niyesa kulowa, mundhu mwina wanichogolela."
8 Yesu wadamkambila, "Ima tenga chika lako ujhiyenda." 9 Pampajha mundhu mmeneyo wadalama, wadatenga chika lake ni kuyamba kuyenda.
Chindhu ichi chidachitika Siku lo Pumulila. 10 Chimwecho Ayahudi wina adamkambila mundhu mmeneyo walamichidwa, "Lelo ni Siku lo Pumulila, thauko likaniza iwe kutenga chika lako."
11 Nambho iye wadaayangha, "Mundhu uyo wanilamicha nde uyo wanikambila, ‘Tenga chika lako, uyende.’ "
12 Ndiipo adamfunjha, "Mundhunji, wakukambila utenge chika lako ujhipita?"
13 Nambho iye siwamamjhiwe mundhu uyo wadamlamicha, ndande Yesu wadato choka pamalo pamenepo ni kusingizikana ni ghulu lalikulu la wandhu.
14 Pambuyo pake, Yesu wadampheza mmeneyo walamichidwa Panyumba ya Amnungu, wadamkambila, "Walama chipano, usadachitanjho machimo, dala sichidakuphezanjho chindhu choipa kupunda."
15 Chimwecho mundhu yujha, wadapita kwakambila achogholeli wa Ayahudi kuti Yesu nde uyo wadamlamicha.
16 Ayahudi adayamba kumchaucha Yesu, ndande wadachita chindhu chimenecho Siku lo Pumulila. 17 Ndiipo Yesu wadayangha, "Atate wanga achita njhito mbaka chipano, nane nifunika nichite njhito."
18 Kuchokana ni mawu yaya, achogholeli wa Ayahudi amafuna njila ya kumpha Yesu, osati kowanangape thauko la Siku lo Pumulila, nambho ndande yokamba kuti Amnungu nde Atate wake, chimwecho iye wadajhichita sawa ni Amnungu.
19 Yesu wadakambila, "Uzene nikukambilani, Mwana siwakhoza kuchita chindhu yokha, icho wachiona Atate wake achita, nde icho Mwana wakhoza kuchichita. 20 Atate amkonda Mwana ni kumlangiza yajha Atate wene achita, ndiipo siwamlangize vindhu vavikulu kupitilila ivi, namwe simudabwe. 21 Ngati umo Atate wahyukicha omwalila ni kwapacha umoyo, chimwecho Mwana wapacha umoyo yao wakonda. 22 Atate siamulamula mundhu waliyonjhe, njhito yonjhe yo lamula wamsiila Mwana, 23 kuti wandhu wonjhe amlemekeze Mwana ngati umo walemekezela Atate. Waliyonjhe uyo siwamlemekeza Mwana siwalemekeza yao amtuma."
24 "Zene nikukambilani, mundhu waliyonjhe uyo wavela mawu yanga ni kwaakhulupilila Amnungu yawo anituma, ali ni umoyo wa muyaya. Sialamulidwa muyaya, nambho wachoka kunyifa ni kulowa kuumoyo. 25 Zene nikukambilani, ndhawi ikujha ni chipano ilipo, yapo omwalila savele mvekelo wa Mwana wa Amnungu, ni anyiyao savele mvekelo saakhale ni umoyo. 26 Ngati umo Atate ali chiyambo cha umoyo, chimwecho ampacha Mwana wao kukhala chiyambo cha umoyo. 27 Chimwecho ampacha ulamuli olanga ndande iye ni mundhu Amnungu watuma. 28 Simudadabwa chindhu ichi, mate yake ndhawi ikujha yapo onjhe anyiyawo ali mviliza savele mvekelo wake, 29 onjhe sahyuke, anyiyawo achita vabwino sahyuke ni kupata umoyo wa muyaya, ni anyiwajha achita voipa sahyuke ni kulangidwa."
30 "Ine sinikhoza kuchita chindhu kwa mbhavu zanga namwene. Ine ni lamula ngati umo nivelela kuchoka kwa Atate, ni lamulo langa ni lo vomelezeka. Pakuti sinifuna kuchita chikondi changa namwene, nambho umo wakondela uyo wanituma."
31 "Ngati nikajhichochela umboni namwene, umboni wanga siukhoza kuvomeleka kuti wa uzene. 32 Nambho walipo mwina uyo wanichochela umboni, chimwecho nijhiwa kuti umboni wake ni wazene. 33 Anyiimwe mdamtuma mundhu kwa Yohana, nayo wadauchocha umboni wa uzene. 34 Ine sinifuna wandhu anichochele umboni, nikamba vindhu ivi kuti muomboledwe. 35 Yohana wadali ngati nyali iyo imawala, namwe mdali tayali kukondwela dangalila la ndhawi yo chepa. 36 Nambho ine nili ni umboni waukulu kupunda kupitilila wa Yohana. Pakuti njhito izo nipota, izo anipacha Atate nizichite, ni vizindikilo ivi nivichita nde ivo vinichochela umboni kuti Atate nde yao anituma. 37 Atate yao anituma nde yao anichochela umboni. Anyiimwe simuda velepo mvekelo wake, kapina kumuona umo ali, 38 ni anyiimwe simuyakhulupilila yayo niyakamba pakuti simwaakhulupilila yawo anituma. 39 Anyiimwe muyapenyechecha Malembo Yoyela kwa kuganizila kuti simpate umoyo wa muyaya kwa kuyapenyechecha, nambho malembo yaya yanichochela umboni ine! 40 Chimwecho simufuna kujha kwanga kuti mpate umoyo."
41 "Ine sinifuna ulemelelo kuchoka kwa wandhu. 42 Nambho ine nikujhiwani kuti mulibe chikondi cha Amnungu mmitima mwanu. 43 Ine najha kwa ulamuli wa Atate wanga, anyiimwe simunilandila, nambho mundhu mwina wakajha ni ulamuli wake mwene, mmeneyo simumlandile. 44 Simukhoze bwanji ku khulupilila ni kwina mkonda kupachana ulemelelo mwachinawene kwa mwachinawene, simfunafuna ulemelelo uwo uchokela kwa Mnungu yokha? 45 Simudaganizila kuti ine sinikupacheni mlandu kwa Atate. Musa uyo mwa mumkhulupilila anyiimwe nde uyo siwakupacheni mlandu. 46 Ngati mdakamkhulupilila Musa, mdakanikhulupilila ni ine, ndande Musa wadalemba nghani zanga. 47 Nambho simuyakukhulupilila yajha wayalemba, sumukhoze bwanji kukhulupilila mawu yanga?"