1 Pambuyo pa yameneyo, Yesu wadaachokela oyaluzidwa wake muchijha la nyanja Tibelia. Wadaachokela chimwechi. 2 Simoni Petulo, Tomaso uyo wamatanidwa Mawila, Nasanaeli mundhu wa ku Kana ya Galilaya, wana awili a Zebedayo ni oyaluzidwa wake wina awili, adali onjhe pamojhi.
3 Simoni Petulo wadaakambila achaanjake, "Nipita kuvuwa njhomba."
Nao adaamkambila, "Tipita taonjhe kuvuwa." Ndiipo adapita, adakwela mbwato, nambho usiku umeneo sadapate kandhu. 4 Malenga kucha, Yesu wadaima mbhepete mwa nyanja, nambho oyaluzidwa sadajhiwe kuti nde Yesu. 5 Ndiipo, Yesu wadaafunjha, "Anyamata wanga, simudapate njhomba yaliyonjhe?"
Adayangha, "Sitidapate kandhu."
6 Yesu wadaakambila, "Chichani khokha bendeka lakwene la bwato simupate njhomba." Ndiipo adaponya khokha bendeka limwelo nambho adalepela kuguza ndande ya kuchuluka kwa njhomba.
7 Chimwecho yujha oyaluzidwa wamakondedwa kupunda ni Yesu, wadamkambila Petulo, "Ekee Ambuye!" Simoni Petulo yapo wadavela kuti Ambuye, wadavala njhalu yake, ndande siwadavale njhalu, ni kujhitaya mmajhi. 8 Nambho anyiwajha oyaluzidwa wina yawo adali pamtunda, adajha pa bwato uku niaguza khokha lojhala njhomba, adali ngati utali mita mia kuchoka pamtunda. 9 Yapo adafika pamtunda adapheza moto wa makala wasonghedwa, njhomba niziochedwa ni bumunda. 10 Yesu wadaakambila, "Majhanazoni njhomba zakumojhi izo mwavuwa."
11 Chimwecho, Simoni Petulo wadakwela mubwato, wadaguza khokha limenelo mbaka kumtunda lidajhala njhomba zazikulu mia imojhi ni hamsi ni zitatu. Atangati njhomba zidachuluka, sizidang'ambe khokha. 12 Yesu wadaakambila, "Majhani mudye chakudya cha umawa." Palibe waliyonjhe uyo wadayesa kumfunjha kuti, "Iwe yani?" Ndande adajhiwa adali Ambuye. 13 Yesu wadajha, wadatenga bumunda, wadapacha, ni zijha njhomba wadachita chimwecho.
14 Imene idali mala ya katatu Yesu kwachokela oyaluzidwa wake pambuyo po hyuka.
15 Yapo adadya, Yesu wadamfunjha Simoni Petulo, "Simoni Petulo mwana wa Yohana! Bwanji, unikonda ine kupitilila anyiyawa?"
Nayo wadayangha, "Etu, Ambuye, mujhiwa nikukondani."
Yesu wadamkambila, "Dyecha gulu la mbelele zanga." 16 Ndiipo Yesu wadamfujhanjho kakawili, "Simoni mwana wa Yohana! Bwanji, unikonda?"
Petulo wadayangha, "Etu, Ambuye, mujhiwa nikukondani."
Yesu wadamkambila, "Sunga mbelele zanga." 17 Wadamfunjha kakatatu, "Simoni mwana wa Yohana! Bwanji, unikonda?"
Petulo wadadandaula kupunda ndande wadamfunjha katatu, "Unikonda?" Wadamkambila, "Ambuye, imwe mujhiwa yonjhe, mujhiwa kuti nikukondani."
Yesu wadamkambila, "Dyecha gulu la mbelele zanga. 18 Zene nikukambila, yapo udali mnyamata udavala wamwene lamba lako mchiuno ni kupita uko ufuna. Nambho yapo siukhale mdala siutambasule manja yako ni mundhu mwina siwakuveke lamba ni kukupeleka uko siufuna kupita." 19 Yapo wadakamba chimwecho, wamalangiza umo siwafele Petulo ni kumpacha ulemelelo Mnungu. Ndipo wadamkambila, "Nichate."
20 Petulo yapo wadang'anamuka, wadamuona yujha wakondedwa ni Yesu wachata, mmeyo nde yujha oyaluzidwa uyo wadagona pamtima pa yesu yapo amadya chakudya ndhawi ya usiku, wadamfunjha Yesu, "Ambuye, yani uyo siwakung'anamukeni?" 21 Petulo yapo wadamuona oyaluzidwa mwinayo, wadamfunjha Yesu, "Ambuye chindhu chanji sichimchokele uyu?"
22 Yesu wadamuyangha, "Ngati nifuna wakhale moyo mbaka yapo sinijhe, iwe ikuusu chiyani? Iwe nichate ine"
23 Chimwecho, nghani idaenela pakati oyaluzidwa wina kuti oyaluzidwa mmeneyo siwamwalila. Nambho Yesu siwadaakambile kuti oyaluzidwa mmeneyo siwafa, nambho, "Ngati nifuna wakhale moyo mbaka yapo sinijhe, iwe ikuusu chiyani? Iwe nichate ine"
24 Mmeneyo nde yujha oyaluzidwa wadayaona yaya ni kuyalemba. Nafe tijhiwa kuti yayo wayakamba ya zene.
25 Kuli ni vindhu vambili ivo wadachita Yesu, ngati yadakalembedwa yonjhe, lina palina, niganiza jhiko silidakakwana kuvisunga vikalakala ivo vidakalembedwa.