1 Afalisayo adavela kuti Yesu wamaachita wandhu ambili kukhala woyaluzidwa wake ni kwaabatiza kusiyana ni Yohana, 2 ata ngati uzene Yesu siwamabatize wandhu iye mwenewake, nambho oyaluzidwa wake nde anyiyawo amabatiza. 3 Chimwecho, Yesu yapo wadavela yameneyo, wadachoka ku Yudea kubwela ku jhiko la Galilaya, 4 muulendo wake idafunika wapitile ku Samaliya.
5 Ndiipo, wadafika ku Sikali, mujhi uwo upezeka Msamaliya, pafupi ni munda ujha Yakobo wadampacha mwana wake uyo wamatanidwa Yusufu. 6 Ndeuko kudali ni chithime cha Yakobo, idali saa sita za usana, nayo Yesu kuchokana ni kulema kwa ulendo, wadapumulila mbhepete mwa chitime.
7 Ndiipo, wamkazi mmojhi kuchokela ku Samaliya wadajha pamenepo kutunga majhi. Yesu wadamkambila, "Nipache majhi nimwe." 8 Ndhawi imeneyo oyaluzidwa wake adapita kumujhi kughula chakudya.
9 Wamkazi mmeneyo wadayangha Yesu, "Iwe Muyahudi, ine Msamaliya! Unipembha bwanji majhi?" Wadayangha chimwecho ndande Ayahudi adalibe mgwilizano ni Asamaliya motumikila vindhu.
10 Yesu wadamuyangha, "Ngati udakajhiwa mbhaso ya Mnungu iye ni yani uyo wakukambila umpache majhi wamwe, udakampembha iye, nayo wadakakupacha majhi yayo siyakuchite ukhale moyo wa muyaya."
11 Wamkazi yujha wadayaangha, "Ambuye, imwe mulijhe msomelo, ni chithime chachitali, siupate kuti majhi ya umoyo wa muyaya? 12 Bwanji, iwe wamkulu kupunda kusiyana ni Ambuye watu Yakobo, uyo wadatipacha chithime ichi? Iye mwene wake ni wana wake ni viweto vake adamwa majhi kuchokela mchitime ichi."
13 Yesu wadayangha, "Waliyonjhe uyo siwamwe majhi yaya siwaonenjho lujho. 14 Nambho uyo siwamwe majhi yayo sinimpache, siwaona lujho muyaya. Majhi yayo sini mpache mkati mwake simukhale viwila va majhi ya umoyo ni kumpacha umoyo wa muyaya."
15 Wamkazi mmeneyo wadakamba, "Ambuye, nipacheni majhi yameneyo sinidaonanjho lujho, ni sinidajhanjho pano kutunga majhi."
16 Yesu wadamkambila, "Mapita ukamtane mmunako ujhe nayo pano."
17 Yujha wamkazi wadakamba, "Nilibe wa mmuna."
Yesu wadamkambila, "Yapo wakamba kuti ulibe wa mmuna wakamba uzene." 18 Ndande udakwatiwa ni wachimuna asano, ni uyo ukhala nayo chipano osati mmunako. Wakamba uzene.
19 Wamkazi yujha wadakamba "Atate, niona kuti imwe amlosi. 20 Azee wathu Asamaliya adaalambila Amnungu pa phili lino, nambho anyiimwe Ayahudi mukamba kuti tikalambile ku Yelusalemu."
21 Yesu wadamkambila, "Iwe maye nikhulupilile, ndhawi siijhe iyo simwalambila Atate wanu pa phili lino, kapina Kuyelusalemu. 22 Anyiimwe Asamaliya mlambila icho simuchijhiwa, nambho ife taajhiwa Amnungu yawo taalambila, ndande uomboli wachokela kwa Ayahudi. 23 Ndhawi ikujha, ni chipano ilipo, wandhu azene yapo samlambile Mnungu kwa kuchogozedwa ni Mzimu ni zene. Amnungu waafuna anyiyao alambila mtundu uwu. 24 Amnungu ni Mzimu, ni wonjhe amlambila afunika kumlambila muchizimu ni zene."
25 Wamkazi mmeyo wadamkambila, "Nijhiwa kuti Mesiya, uyo watanidwa Kilisito, wakujha. Yapo siwajhe siwatijhiwiche kila kandhu."
26 Ndiipo Yesu wadamkambila, "Ine nikamba nawe nde mmeneyo."
27 Ndhawi imweyo oyaluzidwa wake adabwela, adadabwa kupunda yapo adampheza Yesu niwakambana ni wamkazi. Nambho palibe uyo wadamkambila wamkazi, "Ufuna chiyani?" Kapina kumfunjha Yesu, "Ndande yanji ukambana ni wamkazi?"
28 Ndiipo wamkazi yujha wadausia mchuko wake pamwepo, ni kupita kumujhi kwaakambila wandhu, 29 "Majhani mkamuone mundhu uyo wanikambila vindhu vonjhe ivo nachita! Bwanji, ikhozekana kuti iye nde Kilisito?" 30 Chimwecho wandhu adachoka kumujhi, ni kumchata Yesu.
31 Ndhawi imweyo oyaluzidwa wake amampembelela Yesu, "Oyaluza, madyani ata pang'onope."
32 Ndiipo Yesu wadaakambila, "Ine nili ni chakudya icho simuchijhiwa."
33 Oyaluzidwa wake adamfunjha, "Bwanji, pali ni mundhu uyo wampelekela chakudya?"
34 Yesu wadayangha, "Chakudya changa nde ichi, kuchita icho wafuna uyo wanituma ni kuimaliza njhito yake. 35 Anyiimwe mukamba kuti, ‘Yakhalila miyezi inayipe, ndhawi yokolola ikujha!’ Nambho ine nikukambilani, penyani minda vokolola umo vakwimila ndhawi yokolola yakwana! 36 Okolola walandila mkokolo kuchokana ni njhito yake, ni wokolola wakusa vokolola ndande ya umoyo wa muyaya, chimwecho uyo wavyala ni uyo wakolola sakondwele pamojhi. 37 Chimwecho mkambo uwo ukamba, ‘Mmojhi wavyala ni mwina wakolola,’ ni wazene. 38 Ine nakutumani mkakolole vokolola ivo simuvipotele njhito, anyiyawo adapota njhito wina, nambho anyiimwe mpata phindu kuchokana kwa mavuto ya njhito zao."
39 Asamalia ambili amujhi ujha, adamkhulupilila Yesu ndande ya umboni wa maye ameneo yapo wadakambila kuti, "Wanikambila vindhu vonjhe ivo nachita." 40 Chimwecho Asamalila adamchota Yesu adampembha wakhale nao, ndiipo wadakhala pamenepo kwa siku ziwili.
41 Wandhu ambili kupunda adamkhulupilila Yesu ndande ya uthenga wake, 42 adamkambila wamkazi mmeneyo, "Chipano takhulupilila, osati ndande ya mawu yakope, tachinawefe tavela, ni tijhiwa kuti uyu nde muomboli wa jhiko la panjhi."
43 Pambuyo pa masiku yawili Yesu wadachokapo pamenepo ni kupita ku Galilaya, 44 pakuti Yesu wadathokamba padanga kuti, "Mlosi siwapheza ulemu mujhiko lake." 45 Ndiipo yapo wadafika ku Galilaya, wandhu aku Galilaya adamlandila, pakuti naonjho adali pwando la Pasaka. Chimwecho adayaona yonjhe yayo wadachita Yesu ku Yelusalemu pa pwando limenelo.
46 Chimwecho Yesu wadafikanjho mbaka Kukana ya ku Galilaya, kujha wadang'anamula majhi kukhala divai. Kudalipo mchogoleli mmojhi uyo wadali ni mnyamata wake uyo wamadwala kujha ku Kapelinaumu. 47 Chimwecho mchogoleli yujha yapo wadavela kuti Yesu wafika ku Galilaya kuchokela ku Yudea, wadamchota ni kumpembha wakamlamiche mwana wake uyo wamadwala pafupi kumwalila. 48 Yesu wadamkambila, "Ukalepela kuona vizindikilo ni vodabwicha siukhulupilila."
49 Mchogoleli mmeneyo wadamkambila, "Waakulu, pepani tiyeni mwana wanga wakali osafe."
50 Ndiipo Yesu wadamkambila, "Mapita pe, mwana wako walama."
Yujha mundhu wadakhulupilila mawu ya Yesu ni kupita. 51 Yapo wadali mnjila wadapezana ni mbowa zake, zidamkambila, "Mwanawako walama!"
52 Chimwecho wadafunjha ndhawi iyo mwana wadalama, adamkambila kuti, "Jhulo ndhawi ya saa saba za usana, nde yapo wadalama." 53 Ndiipo atate wake mwanayo adakumbukila kuti, ndhawi idali ijha Yesu wadamkambila, "Mwana wako walama." Ndiipo iye ni achabale wake onjhe apakhomo lake adakhulupilila.
54 Ichi chidali chizindikilo chakawili icho wadachichita Yesu, yapo wamachoka ku Yudea kupita ku Galilaya.