1 Chipano nikamba chimwechi olanja wakakhala wakali mwana, siwasiyana ni kapolo, hata ngati chuma chonjhe ni chake. 2 Ndhawi imeneyo wakhala panjhi pa wandhu amlela ni akumsunga mbaka yapo siijhe ndhawi ijha idaikidwa ni atate wake. 3 Chimwecho ni ife yapo tidali tikali wana, nafenjho chichijha tidali ngati wana tidalamuludwa vindhu va jhiko lino. 4 Nambho ndhawi yeneyene yapo idakwana Amnungu adamtuma Mwana wao uyo pajhiko lino la panjhi. Mwana uyo wadabadwa ni wamkazi, mwana mmeneyo wadachgozedwa ni thauko la Musa, 5 waombole anyiwajha achogozedwa ni thauko, dala ife Ayahudi tichitidwe kukhala wana Amnungu.
6 Ndande chipano anyiimwe ni wanawake, Amnungu wautuma mzimu wa mwanawake mmitima mwanu, mzimu uwo utichita kuti timtane Mnungu, "Atate wathu." 7 Chimwecho anyiimwe asati akapolonjho nambho niwana, ni ikakhala anyiimwe nimwana, basi simulandile yonjhe yayo Mnungu waikila wana wake.
8 Kale yapo simmamjhiwe Mnungu, chimwecho mmatumikila minungu iyo idali asati Mnungu wa zene. 9 Nambho saino pakuti mwamjhiwa Mnungu, kapina tikambe Mnungu wakujhiwani, mkhoza bwanji kubwela kutumikila thauko ni chikalidwe cha jhiko lino ni kufuna kuvitumilanjho? 10 Mkali kuchita pwando la siku, mwezi, nyengo ni vyaka. 11 Nikhaikila kuti ikhozekena njhito ijha nidaichita kwa anyiimwe, ikhozeka kuti yandotaika chajhe!
12 Achabale nikupembhani mkhale ngati ine, simudachogozedwa ni thauko ngati ine umo nili. Yapo nidali kwanu simdanichitile choipa chilichonjhe. 13 Anyiimwe mjhiwa kuti utenda wanga ndeuwo udanichita nilalikile Uthenga wa Bwino kwa mala yoyamba. 14 Ata chimwecho ndhawi ijha simdaninyoze kapina kunikana ndande ya utenda wanga, ata ngati wina adakukambilani mchite chimwecho, nambho mdanilandila ngati mtumiki wa kumwamba wa Amnungu, ngati Kilisito Yesu mwene. 15 Myambo mdali wandhu okondwela, ndande chipano simkondwela? Nilumbila kuti ndhawi ijha mdakakoza ata kuyazula maso yanu ni kunipacha ine. 16 Bwanji, saino nakhala mdani wanu ndande ya kukukambilani uzene? 17 Achameneo wandu wina ajhichaucha ndande yanu, nambho sakuganizilani bwino. Afuna kukupatulani ni ine kuti anyiimwe mchauchichike ndande yao. 18 Uzene ni chindhu chabwino kupunda kwachitila wandhu wina vindhu vabwino, mchite chimwecho masiku yonjhe ata ngati nili Patali namwe. 19 Wana wanga, ngati mujha wavutikila maye uyo wali ni pathupi ndhawi yojhimasula, niine nivutika ndande yanu mbaka ukhalo yapo siuoneke mkati Kilisito. 20 Ngati nidakakala ni anyiimwe saino, nidakakamba kwa upole pakati panu! Pakuti nikhaikila kupunda ndande ya anyiimwe!
21 Nikambileni, anyiimwe mkonda kulamulidwa ni thauko, bwanji mwavela umo likambila thauko? 22 Yalembedwa mmalembo ya Mnungu kuti Abilahimu wadali ni wana awili, mmojhi wadabala ni wamkazi uyo wadali kapolo ni mwina wadabala kwa mkazake mfulu. 23 Yujha wadabala ni kapolo wadabadwa ngati umo abadwila wina, nambho yujha wadabala ni mkazake mfulu wadabadwa kuchokana ni mujha wadakambila Mnungu. 24 Vindhu vimenevo vidali chifani, anyamaye awili ameneo ni chifani cha mapangano yawili, loyambila nilijha lidachitika kuphili ilo litanidwa sinai, ilo Ajhili ni wanawake wadabalila ku ukapolo. 25 Ajhili wali ngati phili la sinai ilo lili kwa Waalabu, ni chifani cha Mujhi wa Yelusalemu cha chipano, uwo uli kuukapolo pamojhi ni wana wake. 26 Nambho Yelusalemu ya kumwamba ni mujhi uwo siuli kuukapolo, nawo ni chifani cha maye wathu. 27 Pakuti yalembedwa,
"Kondwela iwe wamkazi siubala,
kweza mvekelo iwe siudajhimasulepo mwana,
pakuti wana a yujha wasiidwa niambili,
kupitilila wa yujha wali ni wammuna."
28 Chipano achabale wanga, anyiimwe ni wana a Mnungu kuchokana ni mujha wadakambila, ngati umo idali kwa Isaka. 29 Nambho ngati mujha siku zijha yujha mwana wadabadwila kwa njila iyo yazoeleledwa, wadamvutichya yujha mwana wadabadwa kwa mbhavu za Mzimu wa Mnungu, chimwecho nde umo ichitikila mbaka chipano. 30 Nambho malembo ya Mnungu yakamba bwanji? Yakamba chimwechi, "Mtopole wamkazi kapolo pamojhi ni mwana wake, pakuti mwana wa wamkazi kapolo siwalanjilatu pamojhi ni mwana wa wamkazi uyo osati kapolo." 31 Chimwecho achabale wanga, ife asati wana a wamkazi kapolo, ife ni wana wa wamkazi uyo asati kapolo.