1 Nichatizeni ine ngati umo ine nimchatiza Kilisito.
2 Nikuyelekelani ndande mwanikumbukila mu vindhu vonjhe ni kuyachata mayaluzo nidakupachani. 3 Nambho nifuna mjhiwe kuti Kilisito wali ni ulamuli kwa kila wammuna, ni wammuna wali niulamuli kwa mkazake, ni Mnungu wali ni ulamuli kwa Kilisito. 4 Chimwecho wammuna yapo wapembhela, kapina kuchocha ulosi uku wavinikila mutu mmeneyo siwamlemekeza Kilisito. 5 Ni wamkazi waliyonjhe yapo wapembhela, kapina kulalikila Uthenga Wabwino, popande kumanga njhalu kumutu wake mmeneyo siwamlemekeza mmunake, uyo wachita chimwecho walingana ni wamkazi uyo wameta mpala. 6 Ngati wamkazi siwadamange njhalu kumutu, basi wasenge machichi. Ningati ninjhoni wamkazi kupupa, kapina kumeta mpala, basi mbasa wamange njhalu kumutu. 7 Nambho wammuna siwadavinikila mutu, ndande iye ni chifani ni ulemelelo wa Mnungu. Nambho wamkazi ni chifani cha wammuna, 8 ndande imeneyo, wammuna siwadaumbidwe kuchokela kwa wamkazi, nambho wamkazi waumbidwa kuchokela kwa wammuna. 9 Wammuna siwadaumbidwe kuthangatila wamkazi, nambho wamkazi ndeuyo wadaumbidwa kumthangatila wammuna. 10 Chimwecho nde ndande wamkazi wamanga njhalu mutu wake, ikhale chizindikilo pamwamba pa ulamuli uli pamwamba pake, ndande ya kwa akondwecha atumiki akumwamba Amnungu. 11 Atamchimwecho, pachogolo pa Ambuye, wamkazi wamkhulupilila wammuna, nayo wammuna wamkhulupilila wamkazi. 12 Ngati mujha wamkazi waumbidwa kwa wammuna, nambho wammuna wabalidwa ni wamkazi, Mnungu nde uyo wachita vonjhe.
13 Lamulani mwachinawene, ngati nibwino wamkazi wampembhe Mnungu popande kumanga njhalu kumutu. 14 Ata maumbidwe yene yatiyaluza kuti wammuna kukhala ni machichi ya mbili ninjhoni. 15 Nambho wamkazi wakakhala ni machichi yambili ni ufulu kwaiye. Nde ndande wapachidwa machichi yayatali dala yamvinikile. 16 Ngati mundhu wafuna kulimbana pa mwamba pa chindhu ichi, ndiipo wajhiwe kuti ife wala gulu la wandhu a Mnungu sitiijhiwa kuti umeneo nde mthethe wathu.
17 Yapo niendekela kukuninghani maagizo yaya sinikhoza kukuyelekelani panghani yaya yachatila, Yapo mphezana kumlambila Mnungu anyiimwe mwakhulupilila zenedi vindhu voipa nde vichokela kupitilila vindhu vabwino. 18 Choyamba, navela yapomkomana pamojhi ngati gulu la wandhu amkhulupilila Yesu nivela mupatulana, nane nikhulupila pang'ono. 19 Mate yake ifunika pakhale nikupatulana pakati panu, dala kulangiza kuti achiyani yawo akhulupilila Yesu azene. 20 Zene yapo mkomana pamojhi, nambho simukudya chakudya cha Ambuye. 21 Pakuti kila mmojhi wakudya chakudya chake popande kudya ni mnjake, mbaka akumojhi wanu akhala ni njala, kapina akhala bila chakumwa, nambho wina akudya ni kumwa mbaka kulojhela. 22 Bwanji simkhoza kudya ni kumwa kumakomo yanu? Kapina mudelela gulu la wandhu amkhulupilila Kilisito, ni kwalengecha njhoni anyiyao alibe kandhu? Nikukambileni chiyani? Nikuyelekeleni? Notho osati kwa yameneyo!
23 Pakuti ine nidalandila kwa Ambuye yajha mayaluzo nidakupelekelani, kuti usiku ujha Ambuye Yesu, yapo wadachochedwa wadatenga bumunda, 24 wadamuyamika Mnungu, wadaubandhula, wadakamba, "Ili nithupi langa, ilo lachochedwa ndande yanu. Chitani chimwechi kwa kunikumbukila." 25 Chimwechijha, pambuyo pakudya wadatenga chiko niwakamba, "Chikho ichi ni chipangano cha chipano cha Mnungu, chichimikizidwa kwa mwazi wanga. Chitani chimwechi kila yapo mkumwa, kwa kunikumbukila."
26 Pakuti kila yapo simujhidya bumunda ili ni kumwa mchikho ichi, muuzila wina Ambuye adafa ndande yanu mbaka yapo siwajhe. 27 Chimwecho, kila uyo wakudya bumunda la Ambuye, ni kumwa mchikho ichi ngati umo siifunikila, siwakhale wachita machimo kwa thupi ni mwazi wa Ambuye. 28 Ifunika, mundhu wajhipenyecheche mwene, ukali osadye bumunda ni kumwa mchikho. 29 Pakuti mundhu uyo wakudya ni kumwa, popande kujhiwa mate ya thupi la Ambuye, kwa kuchita chimwecho Mnungu siwakulange. 30 Nde ndande ambili pakati panu ali odwala ni ofooka, ni wina mbaka amwalila. 31 Nambho ngati tidakajipenyechecha bwino tikali osadye, Mnungu siwadaka tilamula. 32 Nambho yapo tilamulidwa ni kulangidwa ni Ambuye tijhikhala ni ulemu, ili sitidalangidwa pamojhi ni wandhu samkhulupilila Yesu.
33 Chimwecho, abale wanga, yapo mkomanika kudya Chakudya cha Ambuye mjhilindana. 34 Mundhu wakakhala ni njala, wadye kukhomo lake, dala kukomanikana kwanu sikudakhala ndande ya kulamulidwa, ninghani ya yayo yakhalila sinikuyangheni yapo sinijhe kwanu.