1 Navela kuti kwanu kuli chigololo, ni chigololo icho sichidakhalepo ata kwa wandhu yao siamjhiwa Mnungu, nakambilidwa pakati panu mmojhi wakhala ni wamkazi wa atate wake. 2 Namwe mujhidama, bwanji ata simudandaula, nikumchocha pakati panu mmeneyo wachita chigololo chimenecho. 3 Atangati sinili pamojhi nianyiimwe pamenepo panu, nambho nikhala naanyiimwe mu mzimu, ine natho mlamula mundhu uyu wachita chigololo ngati nidaka khalapo. 4 Mate yake, zene yapomsonghanika kumlambila Ambuye wathu Yesu nane nikhalapo pamojhi namwe mu mzimu ni kukhoza kwa Ambuye Yesu ukakhalapo. 5 Mpacheni mdani wa Mnungu mundhu mmeneyo dala walibule thupi lake dala wamchite mumndhu mmeneyo wasiye machimo yake, dala mzimu ulamichidwe pa siku la Ambuye.
6 Kujhidama kwanu osati kwabwino, simujhiwa mkambo ukamba, "Amila yochepa itutumucha ufa onjhe wangano." 7 Ndiipo, mkachoche amila ijha ya kale ya machimo, mkhale achipano. Ngati mujha mudali mkali asatilidwe amila. Mate yake Pasaka wathu, watho chochedwa kukhala njhembe, yaani Kilisito. 8 Chimwecho tichite pwando la Pasaka, nambho osati kwa mabumunda ya kale ya amila ya machimo ni voipa, nambho tidye bumunda ilo lilibe amila, bumunda la uzene ni amila yabwino.
9 Nidakulembelani mu kalata yanga kuti msadagwilizana ni wandhu achigololo. 10 Sinikamba msadasinghizikana ni achigololo, kapina okhumbila, anghungu, kapina alambila viboliboli. Pakuti idakafunika kuchoka mujhiko lino. 11 Nambho chipano vindhu umovili nidakulembelani msadasinghizikana ni mundhu wakhulupilila ngati waendekela kuchita machimo, okhumbila, niuyo walambila viboliboli, kapina otukwana kapina olojhela, kapina olanda, mundhu wa mtundu uwu simdavomela ata kudya nayo.
12 Ili ni mate yanji kwalamula anyiwajha ali kubwalo? Achameneo Mnungu siwalamule. Nambho anyiimwe mufunika kulamula gulu lawandhu amkhulupilia Yesu, ngati umo malembo ya Mnungu yalembedwa, "Chocha wandhu oipa pakati panu." 13 Mnungu siwalamule anyiwajha ali kubwalo. Bwanji, anyiimwe simufuna kwalamula anyiyao ali mugulu la wandhu amkhulupilila Yesu? Ngati umo malembo ya Mnungu yalembedwa, "Chocha mundhu oipa pakati panu."