Publicidade

Mateus 24

Yesu wakambilila kugomoledwa kwa nyumba ya Mnungu

1 Yesu yapo wadatuluka kubwalo kwa nyumba ya Mnungu, yapo wamachoka oyaluzidwa wake adampitila ni adayamba kukamba naye kuusu nyumba ya Mnungu. 2 Yesu wadafujha, "Bwanji, muzipenya izi zonjhe? Zene nikukambilani, palibe ata mwala umojhi uwo siukhalile pamwamba pa wina, kila mwala siugwechedwe panjhi."

Kulaga ni kuvutika

3 Yesu yapo wadakhala pa pili la Mizeituni, oyaluzidwa wake adamchata kwa chisisi, adamfunjha, "Tikambile vindhu ivi sivichike liti? Chizindikilo chanji sichilangize kujha kwako ni mathelo ya jhiko?"

4 Yesu wadaayangha, "Chenjelani kuti mundhu waliyonjhe siwadakunyengani. 5 Pakuti wandhu ambili saajhe kwa jhina langa niakamba, ‘Ine nde Kilisito,’ ni sianyenge wandhu ambili. 6 Simuvele nghani za nghondo ni mbili za nghondo, nambho msadaopa, pakuti yaya yafunika yachokele, nambho mathelo ya jhiko yakali osajhe. 7 Wandhu a jhiko limojhi siabulane ni wandhu ajhiko lina, ni wandhu a ufumu umojhi siabulane ni wandhu a ufumu wina. Sikukhale ni njala yaikulu ni chimtingiza cha ndhaka kujhiko lonjhe. 8 Yaya yonjheya siyakhale ngati kuyamba kwa kuwawa kwa kupweteka kojhimasula mwana."

9 "Ndiipo sakugwileni kuti mvutichidwe ni kuphedwa. Wandhu a maiko yonjhe siyakuipileni ndande anyiimwe ni oyaluzidwa wanga. 10 Nyengo imeneyo, wandhu ambili yawo anikhulupilila siasiye kunikhulupilila, ni kung'anamukana ni kuipilana. 11 Siachokele alosi ambili amthila, ni anyiiwo siwanyenge wandhu ambili. 12 Ndande ya kuchuluka kwa volakwa, chikondi cha wandhu ambili sichichepe. 13 Nambho uyo siwalimbe mbaka pothela, nde uyo siwaomboledwe. 14 Uthenga wa bwino uwu siulalikilidwe jhiko lonjhe lapanjhi kuti wandhu wonjhe a pajhiko avele. Nde mathelo yapo siyajhe."

Masiku ya kuvutika kupunda

15 "Chimwecho mukaona ‘Chindhu choipicha icho chipeleka chiwanangiko chaikidwa pa nyumba ya Amnungu’ icho chidakambidwa ni mlosi Danieli." Chaikidwa pamalo yoyela. Uyo wasoma wajhiwe mate yake! 16 "Chimwecho, wajha ali ku jhiko la Yudea athawile ku phili. 17 Mundhu waliyonjhe uyo wali kubwalo kwa nyumba yake, siwadalowa mkati kutenga chindhu chilichonjhe. 18 Uyo wali ku munda siwadabwela kukhomo kutenga chovala chake. 19 Siavutike wajha ali ni pathupi ni yawo ali ni wana akhanda! 20 Pembhelani kuti kuthawa kwanu kusadakhala nyengo yo zizila kapina Siku Lopumulila! 21 Pakuti nyengo imeneyo sikukhale ni mavuto yayakulu, yayo siyadachokelepo kuyambila jhiko yapo lidaumbidwa mbaka lelo, ni siyachokelanjho mavuto yameneyo. 22 Mnungu wadakayachepecha masiku yameneyo ya mavuto, ngati Amnungu wadakasiya kuzichepecha siku zimenezo, palibe uyo wadakakhoza kuomboka. Nambho ndande ya wandhu wake wasangha, Mungu wazichepecha siku zimenezo."

23 "Mundhu waliyonjhe wakakukambilani, ‘Kilisito wali yapa,’ kapina ‘Wali pajha,’ msadamkhuluphilila. 24 Sikuchokele ni alosi amthila ni wandhu anyiyawo samakambe mthila kuti anyiiwo achi Kilisito. Siamachite vizindikilo ni vodabwicha vavikulu kuti ikakhozeka wakoke ata anyiwajha asanghidwa. 25 Velani, nachogolela kukukambilani nyengo ikali yosafika."

26 "Chimwecho, ngati mundhu waliyonjhe wakukambila, ‘Penya, Kilisito wali kuphululu,’ msadapita kumeneko. Kapina wakakamba, ‘Wali ku chumba,’ msadakhulupila. 27 Ngati mbhambe iyo ing'azikila ku mlengalenga ni kuonekana kumwela, ndeumo siikhalile kujha kwa Mwana wa Mundhu."

28 "Paliponjhe pali chitanda nde yapo zisonghana nghwazi."

Kujha kwa Mwana wa Mundhu

29 "Yakathokutha mavuto ya masiku yameneyo, jhuwa silithilidwe mdima, ni mwezi siung'azikila, ndhondwa sizigwe kuchoka ku mlengalenga, ni mbhavu za kumlengalenga sizitingizidwe. 30 Ndiipo sipachokele chizindikilo cha Mwana wa Mundhu kumlengalenga ni mafuko yonjhe ya pajhiko siyaimbe nyimbo za zaya. Nawo siamuone Mwana wa Mundhu niwajha pamwamba pamitambo ya kumlengalenga, mu mbhavu ni ulemelelo waukulu. 31 Mbetete zazikulu sizipulizidwe, ni iye siwaatume atumiki wake akumwamba ku njhonga zinayi za jhiko lapanjhi. Anyiiwo saike pamojhi wandhu wake yawo asanghidwa kuyambila dela limojhi la jhiko mbaka kudela lina."

Yaluzo la mtengo uwo utanidwa mtini

32 "Jhiyaluzeni chifani ichi kuchokela kwa mtengo wa mtini, ndhawi zake yapo ziyamba kuphukila ni kuchocha machamba, mjhiwa kuti nyengo ya mwavu yawandikila. 33 Mchimwechonjho, yapo simuone vindhu vonjhevi, jhiwani kuti ndhawi yakujha Mwana wa Amnungu yawandikila. 34 Zenedi nikukambilani, mbadwa uwu siumwalila mbaka yaya yonjhe yapo siyachokele. 35 Kumwamba ni pajhiko sivipite, nambho mau yanga siyapita ata pang'ono."

Palibe uyo wajhiwa siku kapina saa yobwela Mwana wa Mundhu

36 "Palibe mundhu waliyonjhe wajhiwa siku kapina saa ilo siwajhe, osati atumiki akumwamba kapina Mwana, nambho Atate okha nde yawo ajhiwa. 37 Kujha kwa Mwana wa Mundhu sikulingane ni chijha chidachokela nyengo ya Nuhu. 38 Pa masiku yameneyo ikali osachokele vula ya ikulu, wandhu amadya ni kumwa, waachimuna ni wachikazi amakwata ni kukwatiwa, mbaka yapo Nuhu wadalowa mkati mwa chombo. 39 Wandhu achameneo siamajhiwe chalichonjhe icho sichichokele. Vula yambili idagwa ni kwaapha wandhu wonjhe. Chimwecho ndeumo siikhalile yapo siwabwele Mwana wa Mundhu. 40 Nyengo imeneyo, waachimuna awili sakhale nialima mmunda, mmojhi siwatengedwe, mwina siwasiidwe. 41 Wachikazi awili siakhale pambhelo naapela chakudya, mmojhi siwatengedwe, mwina siwasiidwe. 42 Chimwecho mjhipenyelele, pakuti simujhiwa siku lanji ilo siajhe Ambuye wanu. 43 Ngati mwene nyumba wadakajhiwa siku lakujha mnghungu, siwadaka gona, siwadakamsiya mnghungu waigomole nyumba yake. 44 Chimwecho anyiimwe namwenjho mjhipenyelele, ndande Mwana wa Mundhu siwajhe saa ilo anyiimwe simulijhiwa."

Mbowa wokhulupilika ni wosakhulupilika

45 Yesu wadaendekela kukamba, "Yani wali mbowa wokhulupilika ni wanjelu? Ni mbowa yujha mbuye wake wamuika kwaimilila mbowa wina, ni kwaapacha chakudya pa saa yabwino. 46 Siwakondwele mbowa yujha mbuye wake yapo siwabwele ni kumpheza niwachita chimwecho. 47 Zene nikukambila, mkulu wake siwamuike mbowa mmeneyo kukhala woimilila chuma chake. 48 Nambho ngati mbowa mmeneyo ni woipa ni wakajhikambila mwene wake, ‘Wamkulu wanga siwachedwe kubwela,’ 49 ni kuyamba kwabula mbowa achanjake ni kudya ni kumwa pamojhi ni olojhela. 50 Wamkulu wa mbowa yujha siwabwele pa siku ilo siwadaliyembekeze ni pa saa ilo siwadalijhiwe. 51 Wamkulu wake mundhu yujha siwamlange kupunda ni kumwika pa gulu limojhi ni wandhu yao samvela. Kumeneko sikukhale chililo ni kukukuta mano."

Veja também

Publicidade
Bíblia Online Bíblia Online

Bíblia Online • Versão: 2026-06-18_14-04-22-