1 Yapo yadapita masiku sita, Yesu wadaatenga Petulo, Yakobo ni Yohana mbale wa Yakobo, wadaatenga anyiiwo okha nikupitanao pa pamalo ya chisisi. 2 Kumeneko, Yesu wadang'anamuka nghope pamaso pawo, nghope yake idali yophulikila ngati jhuwa ni njhalu zake zidali zoyela mbee. 3 Ndiipo, Musa ni Eliya adaatulukila pachogolo pao, adakamba ni Yesu. 4 Ndiipo Petulo wadamkambila Yesu, "Ambuye, siikhale bwino ngati sitikhale pano! Ngati mukonda sinimange visakasa vitatu, chimojhi chanu, chimojhi cha Musa ni chimojhi cha Eliya."
5 Petulo yapo wamakamba chimwecho, mtambo wong'azikila udavinikila, ni mvekelo udaveka kuchoka kumtambo, "Uyu nde Mwana wanga uyo nimkonda, nikondwela nayo kupunda, mveleni iye."
6 Oyaluzidwa wake yapo adavela mvekelo ujha adagwa chifufumimba, adaopa kupunda. 7 Yesu wadaachata ni kwaagafya, wadaakambila, "Ukani, msadaopa!" 8 Yapo adapenya, sadamwuone mundhu mwina waliyonjhe, nambho Yesu yokhape.
9 Yapo amachika phili, Yesu wadanyindila, "Msadaakambila wandhu wina yaya mwayaona mbaka yapo Mwana wa Mundhu siwahyuke."
10 Oyaluzidwa wake adaamfunjha, "Ndande yanji oyaluza a thauko akamba kuti Eliya ifunika wajhe uti?"
11 Yesu wadaayangha, "Zenedi, Eliya siwajhe uti, nayo siwavichite vindhu vonjhe kuti vikhale tayali. 12 Nambho nikukambilani, Eliya wathokujha ni anyiiwo siadamjhiwe, ni anyiiwo adamchita umo adafunila. Chinchijha, Mwana wa Mundhu siwavutichidwe mmanja mwao."
13 Ndiipo oyaluzidwa adajhiwa kuti wamaakambila nghani za Yohana Mbatizi.
14 Yapo adafika pa gulu la wandhu, mundhuu mmojhi wadamchata Yesu, wadamgwadila, 15 wadamkambila, "Ambuye mnilengele lisungu, mwanawanga wali ni njilinjili, ni wavutika kupunda. Ndhawi zambili wagwela pamoto kapina mmajhi. 16 Nidampeleka kwa oyaluzidwa wako nambho siadakhoze kumlamicha."
17 Yesu wadaayangha, "Imwe mbadwa wopande chikhulupi ni olakwa! Sinikhale ni anyiimwe mbaka liti? Sinikulimbileni mtima mbaka liti? Jhinayoni pano mnyamatayo." 18 Ndiipo Yesu wadachinyindila chiwanda, nacho chidamchoka mnyamata, ni wadalama pampajha.
19 Ndiipo oyaluzidwa adamchata Yesu kwa yokha, adaamfunjha, "Ndande yanji ife tidalepela kutopola chiwanda chijha?"
20 Yesu wadaayangha, "Ndande ya chikhulupi chanu chochepa. Nikukambilani uzene, ngati mdakakhala ni chikulupi ngati mbeu ya aladali, mdakakhoza kulikambila phili ili, ‘Chokapo upite yapo’ nalo udakapita. Palibe chindhu icho sichilepeleke kwanu. 21 Chiwanda cha mtundu uwu sichikhoza kuchochedwa kwa njila iliyonjhe, nambho kwa kumanga ni kupemdhela."
22 Siku limojhi yapo adali pamojhi kujha ku Galilaya, Yesu wadaakambila, "Mwana wa Mundhu siwagwilidwe ni kupelekedwa kwa wandhu. 23 Anyiiwo saamphe, nambho siku la katatu siwahyuke."
Ni oyaluzidwa wake sadandaule kupunda.
24 Yesu ni oyaluzidwa wake yapo adafika ku Kapelinaumu, wandhu alandila nsongho wa mnyumba ya Mnungu adamchata Petulo ni kumfunjha, "Bwanji, oyaluza wanu wachocha nsongho wa mnyumba ya Mnungu?"
25 Petulo wadayangha, "Yetu, wachocha."
Petulo yapo wadalowa mkati, Yesu wadayamba kumfunjha, "Simoni, iwe uona bwanji? Mafumu ajhiko alandila malipilo ni nsongho kuchoka kwa ayani? Kwa wandhu wao kapina kuchokela kwa alendo?"
26 Petulo wadamuyangha Yesu, "Kuchoka kwa alendo."
Yesu wadamkambila, "Ni bwino, wandhu wao saafunika kuchocha nsongho. 27 Nambho sitifuna kwaakwiicha wandhu anyiyawa, pita kunyanja ukawejhe, utenge njhomba yoyamba kukodwa, uiyasamiche kamwa lake, ni mkati mwake siukomane ndalama. Itenge ukalipile nsongho yaine ni ukajhilipile iwe."