Publicidade

Mateus 28

Kuhyuka kwa Yesu

1 Siku Lopumulila yapo lidata, umawamawa siku la juma pili Maliya wa ku Magidala ni Maliya mwina yujha adapita kupenya pa chiliza. 2 Kwa chizulumukila, kudali chimtingiza chachikulu, mtumiki wa kumwamba wa Amnungu wadachika kuchokela kumwamba adapita kuchiliza ni kuugadabula mwala ujha ni kuukhalila. 3 Mtumiki wa kumwamba yujha wamang'azikila ngati mbhambe, ni njhalu zake zidali zoyela mbee. 4 Alonda wajha adaopa kupunda, amatendhemela ni adaoneka ngati amwalila.

5 Mtumiki wa kumwamba wa Mnungu wadaakambila wachikazi wajha, "Msadaopa! Nijhiwa kuti mumfunafuna Yesu uyo wadapachikidwa pamtanda. 6 Palibemo muno, wathohyuka ngati mujha iye wadakambila. Majhani mpenye malo yayo adamuika. 7 Pitani msanga mkaakambile woyaluzidwa wake kuti, ‘Yesu wahyuka, nayo wakuchogolelani kupita ku Galilaya, kumeneko nde uko simkamuone!’ Kumbukilani icho nakukambilani."

8 Chimwecho waachikazi wajha adachoka pachiliza uku niaopa ni kukondwela, adathamanga kupita kwaakambila oyaluzidwa wake nghani zimenezo.

9 Pampajha, Yesu wadapezana nao, wadaakambila, "Moni!" Waachikazi wajha adamsendelela ni kumgwila myendo yake, adamlambila. 10 Ndiipo Yesu wadaakambila, "Musadaopa! Pitani mkaakambile acha abale wanga apite ku Galilaya, ndeuko siakanione."

Alonda akamba icho chidachokela

11 Wachikazi yapo adali mnjila, alonda akumojhi yawo amalonda chiliza adabwela ku mujhi ni kwaakambila wakulu wa ajhukulu vindhu vonjhe ivo vidachokela. 12 Ajhuku wa akulu adakomana ni akulu adavomelezana chindhu, adaapacha alonda wajha ndalama zambili, 13 adaakambila, "Kambani, ‘Oyaluzidwa wake adajha usiku kuba chitanda chake ife yapo tidagona.’ 14 Nghani izi zikamfikila mlamuli, ife sitikambe naye nianyiimwe simlowa mavuto."

15 Alonda adalandila ndalama ni adachita ngati mujha adakambilidwa. Mbili iyi idaenela kwa Ayahudi mbakana lelo.

Yesu waatulukila oyaluzidwa wake

16 Ndiipo oyaluzidwa khumi ni mmojhi adapita ku Galilaya, kuphili uko Yesu wadaakambila apite. 17 Yapo adamuona Yesu, adamlambila, uku wina ni amukhaikila. 18 Yesu wadajha pafupi pao ni kwaakambila, "Napachidwa ulamulilo wa kuchogoza kumwamba ni jhiko lapanjhi. 19 Chipano pitani kwa wandhu maiko yonjhe, mkaachite kukhala oyaluzidwa, mkaabatize kwa jhina la Atate ni la Mwana ni la Mzimu Woyela, 20 ni mwaayaluze kuyagwila yonjhe yayo nakulamulilani. Zenedi, ine nili pamojhi namwe muyaya mbaka mathelo ya jhiko la panjhi."

Veja também

Publicidade
Bíblia Online Bíblia Online

Bíblia Online • Versão: 2026-06-18_14-04-22-