1 Yesu ni oyaluzidwa wake yapo adawandikila ku Yelusalemu ni kufika kuchijhijhi cha Besifage, ku phili la Mizeituni, wadaatuma oyaluzidwa wake awili amchogholele, 2 wadaakambila, "Pitani mbaka chijhijhi icho chili mchogolo mwanu, simumpheze phunda wamangidwa pamojhi ni mwana wake. Amasuleni ni mnipelekele pano. 3 Mundhu wakakufunjhani chalichonjhe, mkambileni Ambuye amfuna, nayo siwakuloleni mchoke nawo."
4 Vindhu ivi vidachitika kuti yakwanile yajha kambidwa ni mlosi, niwakamba,
5 "Mkambileni mwali wa Sayuni,
‘Penya, mfumu wako watokujhela!
Mpole ni wakwela pamsana pa phunda,
mwana wa phunda.’ "
6 Chimwecho oyaluzidwa wake adapita kuchita ngati mujha Yesu wadakambila. 7 Adampeleka yujha phunda pamojhi ni mwana wake, adayala njhalu pamsana pa mwanaphunda ni Yesu wadakhala pamwamba pake. 8 Gulu lalikulu la wandhu lidayala njhalu zao mnjila ni wandhu wina adadula ndhawi zazing'onozing'ono za mitengo ni kuziyala mnjila. 9 Gulu la wandhu lidachogolela ni lijha limamchata mbuyo lidakweza mvekelo nilikamba, "Watamandidwe Mwana wa Daudi! Wamwawi yujha wakujha kwa jhina la Ambuye! Matamando kwa Mnungu kumwamba!"
10 Yesu yapo wamalowa kumujhi wa Yelusalemu, gulu lonjhe lidadabwa ni kufunjhana, "Uyu ni yani?"
11 Lijha Gulu la wandhu lidayangha, "Uyu nde Yesu mlosi wa Mnungu, wachokela kumujhi wa Nazaleti mmujhi mwa Galilaya,"
12 Yesu wadafika panyumba ya Mnungu ni kwatopola onjhe amagulicha ni kugula, ni kuzigadabula meza zong'anamulila ndalama ni mipando ya anyiwajha amagulicha nghunda, 13 ni wadaakambila, "Yalembedwa mmalembo yoyela, ‘Nyumba yanga siikhale nyumba ya mapembhelo, nambho anyiimwe mwaichita mbhanga ya olanda!’"
14 Wandhu osapenya ni wandhu andendele, adamchata Yesu panyumba ya Mnungu, ni iye wadalamicha. 15 Waakulu waajhukulu ni oyaluza thauko adakwiya yapo adaona vodabwicha ivo wadachita Yesu, ni umo wana amatanila panyumba ya Mnungu nikukamba, "Watamandidwe Mwana wa Daudi." 16 Chimwecho adamfunjha Yesu, "Bwanji, uvela icho achikamba wana anyiyawa?"
Yesu wadayangha, "Yetu, nivela! Bwanji, simudasome malembo yaya, ‘Kwa kamwa la wana waang'onoang'ono ni akhanda, akutamandani imwe.’ "
17 Yesu waadasiya ni kupita kumujhi wa Besaniya, wadagona kumweko.
18 Umawamawa yesu yapo wamabwela kuchokela ku Besaniya kupita kumujhi, wadavela njala. 19 Wadauona mtengo wa mkuyu mbhepete mwanjila, wadaupitila nambho siwadapate chipacho chilichonjhe, udali ni machambape, wadaukambila ujha mtengo, "Usadapachanjho vipacho!" Pampajha mkuyu ujha udauma.
20 Oyaluzidwa wake yapo adapenya chindhu chijha chidachitika, adadabwa kupunda ni kufunjha, "Ndande yanji mtengo uwu wauma kankamojhi?"
21 Yesu wadakambila, "Zene nikukambilani, ngati simukhulupilile popande kukayikila, mkhoza kuchita osati ichipe nachita pamtengo, nambho mkhoza kulikambila pili ili, ‘Zuka ukajhitaye mnyanja,’ siikhale chimwecho. 22 Mukakulupilila chindhu chilichonjhe simpembhe mmapembhelo, simulandile."
23 Yesu wadapitanjho pa nyumba ya Mnungu ni yapo wamayaluza, waakulu ajhukulu ni waakulu a wandhu adampitlia ni adamfunjha, "Uchita ivi kwa ulamulilo wanji? Yani wakupacha ulamulilo uwu?"
24 Yesu wadaayangha, "Nanenjho nikufunjhani funjho limojhi, ngati simuniyanghe nane sinikukambileni nichita yaya kwa ulamulilo wa yani. 25 Bwanji, ulamulilo wa Yohana wobatiza wandhu udachoka kuti, kumwamba kapina kwa wandhu?"
Adayamba kufunjhana achinawene kwa achinawene niakamba, "Tikakamba, ‘Yachokela kumwamba,’ siwakambe, ‘Ndande yanji simudamkhulupilile Yohana?’ 26 Nambho tikakamba, ‘Yadachoka kwa wandhu,’ tiopa icho sachichite wandhu, pakuti onjhe ajhiwa kuti Yohana wadali mlosi." 27 Chimwecho adamuyangha Yesu, "Sitijhiwa."
Yesu nayo wadakamba, "Nanenjho sinikukambilani kuti nichita yaya kwa ulamuli wa yani."
28 "Muganiza bwanji? Mundhu mmojhi wadali ni wana awili wachimuna. Wadapita kwa yujha wamkulu wadamkambila ‘Mwanawanga lelo mapita ukachite njhito mumunda wa zabibu.’ 29 Iye wadayangha, ‘Sinipita,’ nambho pambuyo wadang'anamula maganizo ni kupita. 30 Ndiipo tate yujha adapita kwa mwana wa kawili adakamba ngati mujha adamkambila oyambila, iye wadayangha, ‘Yetu atate,’ nambho siwadapite. 31 Yani wachita yaja amayafuna atate pakati pa wana yawa awili?"
Adayangha, "Yujha oyamba,"
Yesu wadakambila, "Zene nikukambilani olandila malipilo ni mahule siakuchogoleleni kulowa muufumu wa Mnungu. 32 Yohana Mbatizi wadajha kukulangizani umo mfunikila kukhala kwa kwaakwadilicha Amnungu, anyiimwe simuda mkhulupilile, nambho olandila malipilo ni achigololo adamkulupilila. Chimchijha anyiimwe yapo mudaona yameneyo simudalape ni kumkulupilila."
33 Yesu wadaakambila, "Velani chifani china, kudali ni mundhu mmojhi mwene munda wadavyala zabibu mmunda mwake ni kuumangila seli, wadakumba jhenje lofinyila zabibu, wadamanga chilindo ni kwa bwelekecha munda wa zabibu kwa alimi ni iye wadamanga ulendo. 34 Nyengo yokolola idafika, wadaatuma mbowa wake akatenge chakata langa la zabibu kwa wajha alimi kuchokela mmunda mwake. 35 Wajha alimi wadaahundukila mbowa wake ni kumbula mmoji ni kumpa mwina kumbula myala. 36 Yujha mwene munda wadaatumanjho mbowa wina ambili kupitilila wajha oyamba, alimi achameneo adaachitila chimchija. 37 Pothela mwene munda wadaamtuma mwana wake niwakamba, ‘Uyu samlemekeze ndande mwana wanga.’ 38 Nambho wajha alimi yapo adamuona mwanayujha adakambilana, ‘Uyu nde olanja, majhani timphe dala titenge kulanja kwake’ 39 Chimwecho adamuhundukila, ni kumgwila ni kumtaya kubwalo kwa munda wa zabibu ni kumpha."
40 Yesu wadaafunjha, "Yapo siwajhe mwene munda wa zabibu siwachite chiyani wajha alimi?"
41 Adamuyangha, "Siwayomweletu alimi woipa, ni kubwelekecha wina munda wa zabibu, anyiyao siapelekele chakata la zabibu pa nyengo yo kolola."
42 Yesu wadaafunjha, "Bwanji, simudasome mmalembo ya Mnungu,
‘Mwala uwo adaukana omanga
chipano wakala mwala wofunika kupunda pa msingi.
Chindhu ichi chachoka kwa Ambuye,
nalo litidabwicha?’"
43 "Chipano nikukambilani, Ufumu wa Mnungu siulandidwe kwanu ni kwaapacha wandhu wina anyiyawo osati Ayahudi. 44 Ni anyiyawo siagwe pa mwala satyoke vipinjilivipinjili, niuyo siumgwele mwala umeneo siwadimbikedimbike."
45 Waakulu wa ajhukulu ni Afalisayo yapo adavela chifani chimenecho, adajhiwa kuti Yesu wamakamba anyiwo. 46 Chimwecho adafuna njila ya kumgwilila nambho adaopa wandhu ndande wandhu adamkhulupilila kuti Yesu wadali mlosi.