1 Umawamawa, wakulu wa ajhukulu onjhe ni akulu a wandhu adavomelezana kumupha Yesu. 2 Adammanga vingwe ni kumpeleka kwa Pilato, uyo wadali Mloma.
3 Yuda, uyo wadamng'anamuka Yesu, yapo wadaona kuti Yesu walamlidwa kuphedwa, wadandaula ni wadabweza vijha vibandhu selasini va madini ivo vitanidwa ndalama izo wadatenga kwa achogoleli a ajhukulu ni akulu a wandhu. 4 Wadaakambila, "Nalwakwa, pakuti namng'anamuka mundhu wosalakwa kuti waphedwe!"
Anyiiwo adamuyangha, "Ife tilibemo, zako umwene!"
5 Yuda wadazitaya ndalama zimenezo mnyumba ya Mnungu, ndiipo wadachoka ni kupita kujhimangila chingwe mkhosi.
6 Waakulu wa ajhukulu adatondola gelejha za ndalama zijha ni kukamba, "Iyi ni ndalama ya mwazi, siiloledwa kusingizana ni njhembe za Mnyumba ya Mnungu." 7 Chimwecho, yapo adamaliza kuvomelezana, adalamula kuzitumila kugulila munda wa oumba mbiya, kuti pakhale malo yozikila alendo. 8 Iyi ndendande munda ujha utanidwa Munda wa Mwazi mbaka lelo.
9 Chimwecho mawu yajha wadakamba mlosi Yelemiya lakwanila, "Siatenge vibandhu selasini za ndalama izo wandhu a ku Izilaeli adavomelezana kulipa ndande ya iye, 10 adatumila ndalamazo kugulila Munda wa oumba, ngati umo wadaagiza Ambuye."
11 Yesu wadaima pachogolo pa wamkulu wa ku Loma, wamkulu mmeneyo wadamfunjha, "Bwanji, iwe nde mfumu wa Ayahudi?"
Yesu wadayangha, "Iwe ukamba." 12 Nambho wakulu a ajhulu ni wakulu adampacha mlandu, Yesu siwadayanghe chindhu.
13 Ndiipo Pilato wadamfunjha Yesu, "Bwanji siuvela milandhu iyi achocha kwaiwe?"
14 Nambho Yesu siwadayanghe ata mau limoji, ni wamkulu mmeneyo wadazizwa kupunda.
15 Kila pwando la Pasaka, wamkulu wa ku Loma wadali ni chikalidwe cha kummasulila mundhu mmojhi wa mndende uyo wamafunika ni wandhu. 16 Ndhawi imeneyo kudali womangidwa mmojhi wadajhiwika kupunda, wamatanidwa Balaba. 17 Wandhu yapo adapezana pamoji, Pilato wadaafunjha, "Mfuna ni mmasulile yani? Bwanji nimmasulile balaba kapina Yesu watanidwa Kilisito?" 18 Pilato wadakamba chimwecho ndande wadajhiwa kuti Ayahudi adampeleka yesu kwake ndande amamuonela njhanje.
19 Pilato yapo wadakhala pampando wa malamulo, mkazake wadampelekela utengha uwo umakamba, "Usamchita chalichonjhe uyu mundhu siwadalakwe, ndande usiku wa lelo nachauchika kupunda mumaloto chifuko cha iye."
20 Nambho wakulu wa ajhukulu ni waakulu a wandhu adalikhwilizila gulu la wandhu limpembhe Pilato wamasulule Balaba ni Yesu waphedwe. 21 Pilato wadaafunjhanjho, "Pakati pa anyiyawa awili, yuti mufuna ni mmasule?"
Adayangha, "Balaba!"
22 Pilato wadafunjha, "Nimchite chiyani uyu Yesu watanidwa Kilisito?"
Onjhe adakamba "Wapachikidwe pamtanda!"
23 Pilato wadaafunjha, "Ndande yanji? Wachita chindhu chanji choipa?"
Adamkambila "Mpachikeni pamtanda!"
24 Pilato yapo wadajhiwa kuti siwakoza kuchita chalichonjhe, ni mkangajhili umatoyamba, wadatenga majhi ni kusamba mmanja, pamaso pa gulu ni wadakamba, "Ine nilibemo pa nyifa ya mundhu uyu, izo zanu mwachina wene!"
25 Wandhu wonjhe adayangha, "Kulakwa kumeneko kwa kumpha Yesu sikukhale kwaife ni wana watu!"
26 Ndiipo wadammasulila Balaba ni adalamula Yesu wabulidwe mikwapulo, wadapacha kuti akampachike pamtanda.
27 Ndiipo asikali a Pilato adampeleka Yesu kuseli kwa nyumba ya mfumu, ndiipo gulu lonjhe la asikali lidamzungulila. 28 Adamvula njhalu zake ni kumveka njhalu ya chifumu. 29 Adasoka nghata ya minga nikumveka kumutu, adamwikila mkwapulo kujanja lake la kwene. Adagwada pachogolo pake ni kumchitila vipongwe uku niakamba, "Moni mfumu wa Ayahudi!" 30 Adamlavulila malovu, adaitenga ijha mkwapulo ni kumbula nawo kumutu. 31 Yapo adamaliza kumchitila chipongwe, adamvula njhalu ijha ya chifumu ni kumveka njhalu zake. Ndiipo adampeleka wakapachikidwe pamtanda.
32 Yapo amachoka, adamkomana ni wammuna wakusilia jina lake Simoni adamkakamiza waubale mtanda wa Yesu. 33 Adapita pamalo patanidwa Goligota mateyake, malo ya Chifuvu cha Mutu. 34 Adampacha divai yali ni ndulu wamwe nambho yapo wadailawa wadakana kuimwa.
35 Adampachika pamtanda ni kugawana njhalu, zake kwa kuzibulila ghudughudu.
36 Adakhala pamwepo kumchita ulonda. 37 Chibao chidali pamwamba pa mtanda wake chidalembedwa chimwechi, "Uyu ni Yesu, Mfumu wa Ayahudi." 38 Anghunghu awili nawo adapachikidwa pamojhi ni Yesu kila mmojhi wadali ni mtanda wake mmojhi kwene ni mwina kumanjele kwake.
39 Wandhu amapita pamenepo, adatingiza mitu yao ni kumtukwana Yesu. 40 Niakamba, "Iwe! Siudajhidama kuti siuligomole nyumba ya Mnungu ni kuimanga kwa siku zitatu? Chipano jhilamiche umwene. Ngati iwe ni Mwana wa Mnungu, chika pamtanda!"
41 Chimchijha wakulu wa ajhukulu ni oyaluza thauko ni waakulu adamchita chipongwe. 42 Adakamba, "Wadalamicha wandhu wina walepela kujilamicha mwene wake! Iye ngati mfumu wa Izilaeli wachike chipano pamtanda, ife sitimkulupilile! 43 Wadamkhulupilila Mnungu wadakamba kuti iye ni mwana wa Mnungu. Chipano tiyeni tione ngati Mnungu siwamuombole."
44 Chimchijha wajha anghunghu awili wadapachikidwa pamojhi niiye, adamtukwana.
45 Kuchokela saa sita mbaka sa tisa usana, mdima udavinikila jhiko lonjhe. 46 Yapo idafika saa tisa, Yesu wadakweza mvekelo, "Eloi, Eloi, lama sabakitani?" Mate yake, "Mnungu wanga, Mnungu wanga, mbona mwanisiya?"
47 Wandhu adaima pajha yapo adavela, adakamba, "Wamtana Eliya!" 48 Kankamojhi, mmojhi wao wadathamanga, wadatenga buula ni kubiza mu divai yowawa, ni wadaika panjhonga pa mkwapulo ni kumapacha Yesu kuti wafifinye.
49 Nambho wina adakamba, "Msiyeni, tione ngati Eliya siwajhe kumuombola."
50 Yesu wadatananjho kwa mvekelo waukulu, wadamwalila.
51 Pampajh, panzia ilo lidapachikidwa mnyumba ya Mnungu, lidang'ambika pakati kuyambila kumwamba mbaka panjhi. Jhiko lidatingizika ni ndhaka idasweka, 52 viliza vidamasuka, ni wandhu ambili a Mnungu yawo adamwalila, adahyuka. 53 Yesu yapo wadahyuka wandhu ambili adachoka mmanda, adalowa ku Yelusalemu mu Mujhi Woyela, wandhu ambili wadaaona.
54 Yujha wamkulu wa asikali, pamojhi ni asikali yawo amalonda chiliza cha Yesu, yapo adaona chimtingiza cha ndhaka ni kila kandhu yako kadachitika, adagwilidwa ni mandha, adakamba, "Zenedi, uyu wadali Mwana wa Mnungu!"
55 Pameneko adalipo waachikazi ambili yawo amapenyecha kwa patali, nde yawo adamchata Yesu kutoka ku Galilaya ni amtumikila iye. 56 Pakati pa wachikazi achameneo adalipo Malia wa kumujhi wa Magidala ni Maliya maye wao wang'ono wachi Yakobo ni Yusufu, pamojhi ni mkazi wa Zebedayo.
57 Ujhulo yapo udajha, wadajha wopata mmojhi kuchokela ku Alimataya, jhina lake Yusufu, Mundu mmeneyo nayo wadali mmojhi wa oyaluzidwa a Yesu. 58 Wadampitila Pilato, wadawenda kuti wapachidwe chitanda cha Yesu. Pilato wadalamula kuti wapachidwe. 59 Ndiipo Yusufu wadatenga chitanda cha Yesu ni kuchiveka sanda, 60 wadachiika chitanda muchiliza chake cha chipano icho wadakumba mundhaka yolimba. Ndiipo wadauvilingicha mwala waukulu pakhomo la chiliza ni kuchokapo. 61 Maliya wa ku Magedala ni Maliya mwina yujha adakhala niapenyechana ni chilizacho.
62 Siku ilo lidachata lidali siku lo Lopumula, ajhukulu wa mkulu ni Afalisayo adampitila Pilato, 63 adamkambila, "Imwe ambuye, tikumbukila yujha mundhu wamthila, yapo wadali wakali wa moyo, wadakamba, ‘Sinihyuke siku la katatu.’ 64 Chimwecho lamulani kuti chiliza chilondedwe kwa masiku yatatu. Popande chimwecho oyaluzidwawake akhoza kujha ni kuba thupi lake ni kwakambila wandhu wahyuka. Unami umenewo wothela siukhale woipa kupunda kusiyana ni ujha woyamba."
65 Pilato wadakamba, "Mulinao alonda, pitani mkalonde chiliza ngati umo mukhozela."
66 Chimwecho adapita ku chiliza pamojhi ni alonda pakuika chidindo pa mwala ni kwaasiya asikali alilonde.