6 ndi kupita kwawo. Kenaka amayitana anzake ndi anansi pamodzi, ndi kuti, ‘Kondwerani nane; ine ndayipeza nkhosa yanga yotayika ija.’ 7 Ine ndikukuwuzani kuti momwemonso kudzakhala chikondwerero chachikulu kumwamba chifukwa cha wochimwa mmodzi amene watembenuka mtima kusiyana ndi anthu olungama 99 amene ali otembenuka mtima kale."
Publicidade
Luka 15:6,7
TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo
Em outras traduções
- NTNYBL2025 Nyanja
6 Yapo wafika kukhomo, waatana achabwenji lake ni majhilani wake ni kwakambila, ‘Tiyeni tikondwele pamojhi, ndande naipata ijha mbelele iyo idasowa.’ 7 Nikukambilani chimwecho, sikukhale chikondwelo chachikulu kumwamba ndande ya mundhu mmojhi wamachimo uyo walapa, kupitilila wandhu tisini ni tisa wovomelezeka pamaso pa Mnungu yawo kulapa."
Direitos das traduções citadas
Estes versículos te tocaram? Ore agora!
+581 estão orando agora.
Junte-se à corrente de oração.